Mbiri za a Mboni za Yehova Ena Zofalitsidwa M’magazini Athu
Gwiritsani ntchito malinki omwe ali m’munsiwa kuti mupeze nkhani zosiyanasiyana zofotokoza mbiri za a Mboni za Yehova ena zomwe zinafalitsidwa kuyambira mu 1955. Mukhoza kupeza nkhanizi zomwe zinalembedwa potengera mayina a anthu kapena mitu ya nkhani zawo.