Khalani Bwenzi la Yehova Uzipilira Ena Akakuchitira Nkhanza YAMBANI Uzipilira Ena Akakuchitira Nkhanza Nthawi zina anthu amatichitira nkhanza. Ndiye tiyenera kutani? Pangani Dawunilodi Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi NKHANI ZOSIYANASIYANA Phunzirani kwa Anzake a Yehova—Zochita Gwiritsani ntchito zochitazi kuti mupangenso zinthu zosiyanasiyana za m’mavidiyo a Phunzirani kwa Anzake a Yehova, ndipo kambiranani ndi ana anu mfundo zomwe mwaphunzira. ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA Zoti Ana Achite Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.