Khalani Bwenzi la Yehova
Munachitira Ine Amene
Tingathandize Akhristu odzodzedwa m’njira zambiri. Tiyeni tione zina mwa njirazi.
Makolo, werengani n’kukambirana ndi ana anu lemba la Mateyu 25:40.
Pangani dawunilodi n’kupulinta.
Mukaonera vidiyo yakuti, Munachitira Ine Amene, kambiranani ndi ana anu njira zosiyanasiyana zolalikirira, zakale ndi zamasiku ano zomwe, ndipo musankhepo njira imodzi yoti muifufuze pamodzi.