KHALANI BWENZI LA YEHOVA
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kumvera Mulungu Ngakhale Sitimamuona?
Pa zinthu zimene Yehova analenga, zomwe timakonda zimatikumbutsa kuti iye amationa komanso kuti zochita zathu zimamukhudza.
Makolo, werengani ndi kukambirana lemba la 1 Yohane 3:22 limodzi ndi ana anu.
Pangani dawunilodi ndi kusindikiza zochitazi.
Zinthu zokongola zomwe Yehova analenga zimatikumbutsa kuti iye amationa komanso kuti zochita zathu zimamukhudza. Pambuyo poonera vidiyo, kambiranani mafunso ndiponso muwerenge vesi lomwe lili patsamba 1. Kenako thandizani ana anu kuti alembe zinthu zomwe amazikonda patsamba 2.