KHALANI BWENZI LA YEHOVA
Uzisangalatsa Yehova
Phunzirani zimene mungachite kuti mukhale wolimba mtima ngati Mateo, yemwe anachita zinthu mosiyana ndi ena ndipo zinasangalatsa Yehova.
Makolo, werengani komanso kukambirana ndi ana anu lemba la Miyambo 27:11.
Pangani dawunilodi ndi kusindikiza zochitazi
Mukamaliza kuonera vidiyo, uzani mwana wanu kuti amalizitse chithunzi pochekenera Mateo pamene mukukambirana naye mafunso ali m’munsiwa. Pakapita masiku angapo, uzani mwana wanuyo kuti alembe zimene anachita kuti asangalatse Yehova.