KHALANI BWENZI LA YEHOVA​—ZOCHITA

Fufuzani Anthu Oyenerera

Chichewa
Fufuzani Anthu Oyenerera
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/501700061/univ/wpub/501700061_univ_sqr_xl.jpg

KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Fufuzani Anthu Oyenerera

Fufuzani Anthu Oyenerera

Mukhoza kutengera chitsanzo cha Yesu komanso atumwi ake pa nkhani yofufuza anthu omwe angamvetsere uthenga wa Ufumu.

Makolo, werengani ndi kukambirana ndi ana anu lemba la Mateyu 10:11.

Pangani dawunilodi n’kupulinta.

Mukaonera vidiyo yakuti Fufuzani Anthu Oyenerera, thandizani ana anu kupeza nsodzi, wokhometsa msonkho komanso mwininyumba. Kenako kambiranani mafunso n’kukonzekera limodzi zomwe mungakachite mu utumiki.