Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Petr Muzny: Pulofesa wa Zamalamulo Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake

Petr Muzny: Pulofesa wa Zamalamulo Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake

Pulofesa Muzny ndi katswiri wa kaganizidwe ka anthu. Kodi mfundo yoti zinthu sizingachitike zokha popanda chochititsa inamupangitsa bwanji kuti ayambe kukayikira zimene ankakhulupirira?