Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Irène Hof Laurenceau: Dokotala Woona za Mafupa Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake

Irène Hof Laurenceau: Dokotala Woona za Mafupa Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake

Irène ankakhulupirira kuti kufanana kwa mmene zamoyo zosiyanasiyana zinapangidwira ndi umboni wakuti zinachita kusintha kuchokera ku zinthu zina. Komabe ntchito yake yoikilira miyendo yochita kupanga, inachititsa kuti ayambe kukayikira zomwe ankakhulupirirazi.