Zachilengedwe Zimatiphunzitsa za Ulemerero wa Mulungu

Zachilengedwe Zimatiphunzitsa za Ulemerero wa Mulungu

Tikamachita chidwi ndi zinthu za m’chilengedwe timaphunzira zambiri zokhudza Mlengi wathu ndipo tikhoza kukhala naye pa ubwenzi wolimba.