Mapatani

Mapatani

Chilengedwechi chili ndi zinthu zambiri zomwe zinapangidwa m’mapatani osiyanasiyana komanso ogometsa. Kodi zinangochitika zokha kuti zikhale choncho kapena zimasonyeza kuti zinapangidwa ndi winawake waluso kwambiri?