Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Madzi

Madzi

Zamoyo zonse zimadalira madzi. Kaya madziwo ndi kadontho kochepa kwambiri kapena ndi ambiri ngati mmene amakhalira m’nyanja, amakhala ndi zinthu zofunika kwambiri ku zinthu zamoyo. Onerani vidiyoyi kuti muone kufunika kwake.