Zachilengedwe Zimatiphunzitsa za Ulemerero wa Mulungu

Tikamachita chidwi ndi zinthu za m’chilengedwechi, timaphunzira za makhalidwe a Mlengi wathu ndipo zimatithandiza kuti tikhale naye paubwenzi.

Zachilengedwe Zimatiphunzitsa za Ulemerero wa Mulungu

Kodi tsiku lililonse mumaona zinthu zachilengedwe zochuluka bwanji? Zachilengedwe zimatithandiza kudziwa kuti Mulungu amatikonda kwambiri komanso kuti ali ndi nzeru zopanda malire.

Kuwala ndi Mitundu ya Zinthu

Mitundu yokongola yomwe Yehova anaika pa cholengedwa chilichonse imatikumbutsa kuti amatikonda kwambiri.

Madzi

Madzi amapereka umboni wamphamvu wotsimikizira kuti Yehova Mulungu ndi Mlengi wanzeru.

Mmene Zamoyo Zinapangidwira

Kodi zamoyo zinapangidwa bwanji? Kodi timaona kuti kudalirana kwa zinthu zamoyo ndi umboni wosonyeza kuti pali winawake amene anazipangitsa?

Mapatani

Mapatani omwe timawaona m’zinthu zachilengedwe sanakhaleko mwaokha. Patani iliyonse inapangidwa mwaluso komanso motsatira ndondomeko inayake.

Zithunzi za Kuthambo

Mlalang’amba wathu ndi wokongola kwambiri. Kodi umatiphunzitsa chiyani zokhudza amene anaulenga?