Pitani ku nkhani yake

‘Uthenga Wabwino Ukulalikidwa Kudziko Lililonse, Fuko Lililonse ndi Chinenero Chilichonse’

Padziko lonse pali zinenero pafupifupi 6,700. Choncho mpofunika kuti uthenga wabwino wa m’Baibulo umasuliridwe m’zinenero zambiri. Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene a Mboni za Yehova akuchita kuti anthu a zinenero zosiyanasiyana amve uthenga wa m’Baibulo.