Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Yohane

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Yohane

Yohane anafotokoza mwamphamvu chifukwa chake kukondana kuli kofunika. Anafotokozanso kuti tizikana zinthu zomwe zingasokoneze ubwenzi wathu ndi Mulungu.