Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mukhoza Kupeza Mabwenzi Kulikonse

Mukhoza Kupeza Mabwenzi Kulikonse

Vidiyoyi ikusonyeza kuti Akil anasiyana ndi anzake omwe ankagwirizana nawo poyamba. Komabe nkhani ya Davide ndi Yonatani yamuthandiza kupezanso mnzake kumalo komwe sankayembekezera.