Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mukamamvera Uphungu Mudzakhala Anzeru

Mukamamvera Uphungu Mudzakhala Anzeru

A Byong Soo akumvetsera malangizo a m’Malemba ngakhale kuti mkulu amene akuwapatsa malangizoyo ndi wachinyamata. A Soo akumvetsera chifukwa akudziwa kuti malangizowo akuchokera kwa Yehova.