Khalani Bwenzi la Yehova

Onani kapena tsitsani mavidiyo ojambula omwe amaphunzitsa ana maphunziro ofunika a Baibulo.

Ukhoza Kuchita Upainiya

Kalebe akuganiza zochita upainiya pambuyo pomva zimene zalengezedwa ku Nyumba ya Ufumu.

Anasonyeza Chikondi Chachikulu Kwambiri

Dziwani chifukwa chake nsembe ndi mphatso yapadera kwambiri imene anthu anapatsidwa.

Zomwe Zili Muvidiyo ya Khalani Bwenzi la Yehova: Yehova Amakuona Kuti Ndiwe Wofunika

Zowe waphunzira kuti kukhala osiyana ndi ena kukhoza kukhala kwabwino.

Ukhale Wofalitsa Wosabatizidwa

Kalebe akuphunzira zimene angachite kuti akhale wofalitsa wosabatizidwa.

Phunziro 47: Ndi Ndani Angakhale Mnzanga?

Yehova amafuna kuti ukhale ndi anzako, koma kodi ungasankhe bwanji anzako abwino?

Phunziro 45: N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kumvera Mulungu Ngakhale Sitimamuona?

Ngakhale kuti sitingathe kuona Mulungu, nanga n’chifukwa chiyani timamumvera? Tiyeni tione mmene Sofiya akuyankhira funso limeneli.

Phunziro 41: Kodi Tiyenera Kukondwerera Mabefide?

Kodi ungathandize bwanji anthu ena kumvetsa chfukwa chake sumakondwerera mabefide?

Phunziro 40: Yehova Amakhululuka

Tikalakwitsa chinachake, kodi tizinyanyala? Tiyeni tione zimene Kalebe waphunzira m’nkhani inayake ya m’Baibulo.

Phunziro 38: Uzikonda Mnzako

Kodi ungatengere bwanji chitsanzo cha Msamariya wachifundo posonyeza chikondi kwa anzako?

Phunziro 37: Kudzimana

Yesu ankadzimana nthawi zonse n’cholinga choti athandize ena. Kodi ungamutsanzire bwanji Yesu?

Phunziro 36: Amatilangiza Chifukwa Chotikonda

N’chifukwa chiyani Yehova amalangiza amene amawakonda?

Phunziro 35: Muzigwiritsa Ntchito Nthawi Mwanzeru

Nthawi ndi mphatso yochokera kwa Yehova. Muziigwiritsa ntchito mwanzeru.

Phunziro 33: Uzisangalatsa Yehova

Zimene mumachita tsiku lililonse zingasangalatse mtima wa Mulungu.

Phunziro 32: Uzichita Zinthu Bwino Muutumiki

Usanapite muutumiki, pali zinthu zitatu zimene uyenera kuzidziwa.

Phunziro 31: Uzikonda Nyumba ya Yehova

Kodi mumagwira nawo ntchito yoyeretsa Nyumba ya Ufumu?

Phunziro 30: Kupirira Imfa ya Munthu Yemwe Munkamukonda

N’chiyani chingatithandize kuti tipirire imfa ya munthu yemwe tinkamukonda?

Phunziro 29: Uzidzichepetsa

Kalebe anazindikira tanthauzo la kukhala wodzichepetsa.

Phunziro 27: Yerekezera Kuti Uli M’Paradaiso

Kodi umadziyerekezera uli m’dziko latsopano?

Phunziro 26: Dipo

Kodi dipo lingatithandize bwanji tikakumana ndi mavuto panopa?

Phunziro 25: Mmene Mungapezere Anzanu

Kodi ndi ndani angakhale mnzanu mumpingo?

Phunziro 24: Yehova Anapanga Zinthu Zonse Modabwitsa

Mulungu anapanga zinthu zambiri zodabwitsa. Kodi inu mumakonda chiyani?

Phunziro 23: Dzina la Yehova

Kodi umadziwa zimene dzina la Mulungu limatanthauza?

Phunziro 22: Mwamuna Mmodzi, Mkazi Mmodzi

Kodi Mulungu anapereka mfundo zotani zokhudza ukwati nanga n’chifukwa chiyani tiyenera kuzitsatira?

Phunziro 21: Ukhoza Kukhala Woleza Mtima

Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene zinamuthandiza Kalebe kuti akhale woleza mtima.

Phunziro 20: Uzinena Zoona

N’chifukwa chiyani nthawi zonse uyenera kunena zoona?

Phunziro 19: Uzikhala Wopatsa

Kodi ndi zinthu zabwino ziti zimene zimachitika chifukwa chakuti atumiki a Yehova ndi wopatsa?

Phunziro 18: Uzilemekeza Nyumba ya Yehova

Kodi mungasonyeze bwanji khalidwe labwino ku nyumba imene timalambiriramo Yehova?

Phunziro 17: Tetezani Ana Anu

Kalebe ndi sofiya akuphunzira zimene angachite kuti akhale otetezeka.

Phunziro 16: Muzilalikira Anthu Olankhula Chinenero cha Dziko Lina

Kodi mungatani kuti mulalikire munthu amene samatha kulankhula chinenero chanu?

Phunziro 15: Muzimvetsera Tikakhala Pamisonkhano

N’chifukwa chiyani tiyenera kumvetsera tikakhala pamisonkhano?

Phunziro 14: Uzikonzekera Zimene Ukayankhe

Kodi ndi zinthu 4 ziti zimene mungachite pokonzekera zimene mukayankhe kumisonkhano?

Phunziro 13: Yehova Akuthandiza Kuti Ukhale Wolimba Mtima

N’chiyani chingakuthandizeni kuti muziuza ena zokhudza Yehova molimba mtima?

Phunziro 12: Kalebe ndi Sofiya Akukaona Malo ku Beteli

Onani Kalebe ndi Sofiya akuona zithunzi ku Beteli. Muonanso ntchito imene imachitika ku Beteli.

Mavidiyo Amakatuni Omwe Ana Akuwakonda Kwambiri

A Mboni za Yehova akupanga mavidiyo amakatuni pofuna kuphunzitsa ana mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’Baibulo. Onani zimene zimachitika pokonzekera mavidiyowa kuti mudziwe mmene amawapangira.

Phunziro 11: Uzikhululuka ndi Mtima Wonse

Kodi munthu akakuchitirani choipa muyenera kumutani?

Phunziro 10: Uzikhala Wokoma Mtima Ndiponso Wopatsa

Onerani kuti mudziwe mmene Kalebe ndi Sofiya amasangalalira akamagawana zinthu.

Phunziro 9: “Yehova . . . Analenga Zinthu Zonse”

Kodi ukudziwa zinthu zimene Mulungu anayambirira kulenga? Onera vidiyoyi kuti udziwe mmene Mulungu analengera zinthu zosiyanasiyana.

Phunziro 8: Uzikhala Waukhondo

Yehova amaika chilichonse pamalo oyenera. Onani zimene nanunso mungachite kuti muzikhala aukhondo

Phunziro 7: Kupatsa N’kwabwino

Pali zambiri zimene mungachite kuti muthandize ena. Kodi mukuganiza kuti mungachite chiyani?

Phunziro 6: Uzipempha Mwaulemu Ndiponso Uzithokoza

Kalebe waphunzira kuti kupempha mwaulemu ndiponso kuthokoza ndi kofunika kwambiri.

Phunziro 5: Tiyeni Tikalalikire

Kodi Sofiya watenga zonse zofunika popita kolalikira? Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene inunso muyenera kutenga popita kolalikira.

Phunziro 4: Kuba N’koipa

Kodi Mulungu amakuona bwanji kuba? Werengani Ekisodo 20:15. Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zambiri limodzi ndi Kalebe.

Phunziro 3: Muzipemphera Nthawi Iliyonse

Vidiyoyi ndi yoti mukhoza kuipanga dawunilodi ndipo imaphunzitsa ana nthawi komanso malo amene angapemphere kwa Yehova.

Phunziro 2: Muzimvera Yehova

Kodi matoyi amene mumaseweretsa angakhale ndi vuto? Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene Kalebe anachita kuti akhale bwenzi la Yehova

Phunziro 1: Muzimvera Makolo Anu

N’chifukwa chiyani kumvera makolo anu kuli kofunika? Onerani vidiyoyi kuti mudziwe chifukwa chake limodzi ndi Kalebe.

Pepani, palibe mawu ofanana ndi omwe mwasankha.