N’chifukwa Chiyani Yesu Anafa?

N’chifukwa Chiyani Yesu Anafa?

Baibulo limasonyeza kuti imfa ya Yesu ndi yofunika kwambiri. Komano kodi imfa yake ili ndi phindu lililonse?