Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Miriamu

Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Miriamu

Miriamu analakwitsa kwambiri zinthu. Koma kenako anasintha mmene ankaonera zinthu ndipo anapitiriza kutumikira Yehova ndi mtima wake wonse.