Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Abulahamu, Mbali Yoyamba
Pa nthawi zosiyanasiyana Abulahamu anasonyeza kuti ankakhulupirira kwambiri Yehova Mulungu wake.
Nkhani Zina
Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Amuna ndi Akazi Otchulidwa M’Baibulo Kukhulupirira MulunguMwina Mungakondenso Kudziwa Izi
MUZIYENDA NDI MULUNGU MOLIMBA MTIMA
Abulahamu—Munthu Woyamba Kumenya Nkhondo za Yehova
Kodi tikuphunzira chiyani kwa Abulahamu pokhala wofunitsitsa kupulumutsa Loti, mwana wa mchimwene wake? Kodi Yehova anamudalitsa bwanji chifukwa cha chikhulupiriro ndi kulimba mtima komwe anasonyeza?
TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO
Abulahamu—“Tate wa Onse Okhala ndi Chikhulupiriro”
Kodi Abulahamu anasonyeza bwanji kuti anali ndi chikhulupiriro? Kodi mukufuna kutsanzira Abulahamu m’njira ziti?
NSANJA YA OLONDA
Sara: “Ndiwe Mkazi Wokongola”
Ali ku Iguputo, akalonga a Farao anaona kuti Sara anali mkazi wokongola. Ndiye kodi mukuganiza kuti zinatha bwanji?
NSANJA YA OLONDA
Sara—Yehova Anamutchula Kuti “Mfumukazi”
N’chifukwa chiyani dzina latsopanoli linali lomuyenera?
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zokuthandizani Pophunzira Baibulo
Sankhani zinthu zokuthandizani pophunzira Baibulo zimene zingapangitse kuphunzira kukhala kopindulitsa komanso kosangalatsa.
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Yambani Kuphunzira Baibulo
Phunzirani Baibulo kwaulere, mochita kukambirana ndi mphunzitsi wanu.

