Kodi Yesu Khristu Ndi Mulungu?

Kodi Yesu Khristu Ndi Mulungu?

Anthu ambiri amaona kuti Yesu anali munthu wotchuka kwambiri. Komano, kodi Yesu ndi Mulungu Wamphamvuyonse? Kapena anali munthu wabwino basi?