Mfundo Zofunika za M'Baibulo—Mavidiyo

Kodi Mulungu Amaotcha Anthu Kumoto?

Chichewa
Kodi Mulungu Amaotcha Anthu Kumoto?
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102020415/univ/art/1102020415_univ_sqr_xl.jpg
ebtv

Kodi Mulungu Amaotcha Anthu Kumoto?

Kodi Mulungu Amaotcha Anthu Kumoto?

Zipembedzo zambiri zimaphunzitsa kuti Mulungu amaotcha anthu oipa kumoto kwamuyaya, anthuwo akamwalira. Koma kodi zimenezi n’zoona?