Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2009

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2009

 Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2009

Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

BAIBULO

Ankalikonda, 6/1

Baibulo la Vatican Codex Ndi Chuma, 10/1

Chuma cha M’nyanja Yaikulu ya ku Central America, 9/1

Kodi Muyenera Kuphunzira Chiheberi ndi Chigiriki? 11/1

Lamoyo Ngakhale M’chinenero Chakufa

Lifika ku Madagascar, 12/15

Limasintha Anthu, 2/1, 7/1, 8/1, 11/1

Linapulumuka Modabwitsa, 11/1

Mafanizo, 5/1

Mbali Ina Inalembedwa M’Chigiriki, 4/1

Mfundo Zazikulu za M’buku la Chivumbulutso​—Gawo 1, 1/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Chivumbulutso​—Gawo II, 2/15

Ndi Lothandiza Masiku Ano, 6/1

Zimene Mungachite Kuti Muzilimvetsa, 7/1

MBIRI YA MOYO WANGA

Kodi Ndingam’bwezere Chiyani Yehova? (R. Danner), 6/15

Mmene Misonkhano Yachigawo Itatu Inasinthira Moyo Wanga (G. Warienchuck), 10/15

“Mngelo wa Yehova Azinga” Anthu Ake (C. Connell), 3/15

Munthu Sakhala ndi Moyo ndi Chakudya Chokha (J. Hisiger), 3/1

Ndikusangalala Ngakhale Kuti Ndine Wolumala (P. Gaspar), 5/1

Ndikuthokoza Yehova Ngakhale Kuti Ndakumana ndi Mavuto (E. Acosta), 6/1

Ndinapeza Cholinga cha Moyo (G. Martínez), 9/15

Ndinayamba ‘Kukumbukira Mlengi Wanga’ Zaka 90 Zapitazo (E. Ridgwell), 7/15

“Njira Ndi Iyi, Yendani Inu Mmenemo” (E. Pederson Yosimbidwa ndi R. Pappas), 1/15

MBONI ZA YEHOVA

Anapeza Chuma Chobisika (Estonia), 8/15

Beteli ya ku Brooklyn Yakwanitsa Zaka 100, 5/1

Chimphepo ku Myanmar, 3/1

Kamtsikana Kowolowa Manja, 11/15

Kodi Mungakatumikire Kumene Kukufunika Ofalitsa Ufumu Ambiri?, 4/15, 12/15

Kodi Mungawolokere ku Makedoniya, 12/15

Kodi ndi Chipembedzo Chachipolotesitanti? 11/1

Kufufuza Munthu Mwakhama, 3/1

Malo Ochititsa Chidwi Osindikizira Mabuku, (Watchtower Farms, U.S.A.) 7/1

Mayi Wosauka Koma Wosangalala, 9/1

Mbewu za Choonadi Zafika Kumadera Akutali (Tuva Republic, Russia), 7/15

Msonkhano Wachigawo Wakuti “Khalani Maso,” 3/1

Muli Olandiridwa (misonkhano), 2/1

Muziona Kuti Abale ndi Alongo Anu Osamva Ndi Ofunika Kwambiri, 11/15

Mwambo Womaliza Maphunziro a Gileadi, 2/15, 9/1

Nkhani ya Onse Yapadera, 4/1

Nyanja Yaikulu ya ku Central America, 9/1

Sizigwiritsa Ntchito Mafano Polambira, 2/1

Ulendo Wokumbutsa Chikale (Amish ku U.S.A.), 12/1

Ulendo Wopita Kutali Kwambiri (Sakha Republic), 6/1

Uthenga Wabwino M’zinenero 500, 11/1

‘Yehova Wawalitsa Nkhope Yake pa Iwo’ (osamva), 8/15

MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU

Amuna, Tsanzirani Chikondi cha Khristu, 5/15

Nchiyani Chingakuthandizeni Kupirira Muutumiki? 3/15

Itai, 5/15

Kodi Chipembedzochi Ndi Changa Kapena cha Makolo Anga? 9/15

Kodi Mapeto Ayenera Kudzakupezani Muli Kuti? 5/15

Kodi Mlongo Akamamasulira Nkhani M’chinenero cha Manja, Ayenera Kuvala Chophimba Kumutu? 11/15

Kodi Mungatumikirenso? 8/15

Kodi Muyenera Kuumirira Zokonda Zanu? 2/15

Kugwirizana Kumathandiza Kuti Banja Lizikula Mwauzimu, 7/15

Kulangiza Ana, 2/1

Kupereka Mokondwera Kuchokera Pansi pa Mtima, 11/15

Kusala Kudya, 4/1

Kusangalala ndi Umbeta, 6/15

Landirani Moyamikira Ndipo Perekani ndi Mtima Wonse, 7/15

Maliro, 2/15

Mapemphero Amene Mulungu Amamva, 2/1

Mariya, 1/1

Ngati Mkazi Kapena Mwamuna Wanu Ali ndi Matenda Aakulu, 11/1

Moyo wa Banja, 11/1

Mukakhumudwitsidwa, 9/1

Mulungu Azikulankhulani Tsiku Lililonse, 8/1

Mulungu Sayankha Mapemphero Ena, 1/1

Musaiwale Yehova, 3/15

Muzigwiritsa Ntchito Ndalama Mwanzeru, 8/1

Muzipatsa Ena Ntchito Zina, 6/15

Ndizipereka Ndalama Zingati? 8/1

“Njira Yopambana” ya Chikondi, 7/15

Otanganidwa Koma Osangalala Potumikira Mulungu, 12/15

Pali “Nthawi Yokhala Chete,” 5/15

Pewani Zosokoneza, 8/15

Thandizani Achinyamata Kuti Akule Bwino, 5/1

NKHANI ZOPHUNZIRA

Achinyamata, Yesetsani Kuti Kupita Kwanu Patsogolo Kuonekere, 5/15

“Amatsatira Mwanawankhosa” Nthawi Zonse, 2/15

Angelo Ndiwo “Mizimu Yotumikira Anthu,” 5/15

Anthu Anayambiranso Kukhala ndi Chiyembekezo cha Moyo Wosatha Padziko Lapansi, 8/15

‘Bwera Ukhale Wotsatira Wanga,’ 1/15

Chikondi cha Khristu Chimatilimbikitsa Kukonda Ena, 9/15

Chilengedwe Chimasonyeza Nzeru za Yehova, 4/15

Fufuzani Chuma Chimene ‘Chinabisidwa Mosamala mwa Iye,’ 7/15

Khalani “Achangu pa Ntchito Zabwino,” 6/15

Khalani Achangu pa Nyumba ya Yehova, 6/15

“Khalanibe M’chikondi cha Mulungu,” 8/15

Khalanibe ndi Chimwemwe Mukamakumana ndi Mavuto, 12/15

“Khalani Maso,” 3/15

‘Khalani Mwamtendere ndi Anthu Onse,’ 10/15

Khalani ndi Chikondi Chimene Sichitha Konse, 12/15

Khalani ndi Maganizo a Khristu, 9/15

Khalani Omvera Ndiponso Olimba Mtima Ngati Khristu, 9/15

Kodi Khristu Anaphunzitsa za Chiyembekezo cha Moyo Wosatha Padziko Lapansi? 8/15

Kodi Mapemphero Anu Amagwirizana ndi Zimene Yesu Anaphunzitsa? 2/15

Kodi Mapemphero Anu Amasonyeza Chiyani za Inuyo? 11/15

Kodi Mumayamikira Zimene Yehova Wachita Kuti Akupulumutseni? 9/15

Kodi Ndinu ‘Mdindo wa Kukoma Mtima kwa m’Chisomo cha Mulungu’? 1/15

Kuphunzira Baibulo Kungathandize Kuti Mapemphero Anu Azikhala Atanthauzo, 11/15

Kupita Kwanu Patsogolo Kuzionekera, 12/15

Kuzindikira Mose Wamkulu, 4/15

Kuzindikira Yesu Monga Davide Wamkulu Ndiponso Solomo Wamkulu, 4/15

Lankhulani Zoona kwa Mnansi Wanu, 6/15

Mabanja Achikhristu, Tsatirani Chitsanzo cha Yesu, 7/15

Maphunziro Ochokera kwa Mulungu Ndi Opambanadi, 9/15

Mdindo Wokhulupirika ndi Bungwe Lake Lolamulira, 6/15

Mesiya Ndiye Njira Yopulumutsira Anthu, 12/15

Mtumiki wa Yehova “Analasidwa Chifukwa cha Zolakwa Zathu,” 1/15

Mulungu Anapereka Chiyembekezo cha Moyo Wosatha Padziko Lapansi, 8/15

Mungakhale ndi Khalidwe Labwino mwa Kutsatira Zimene Yesu Anaphunzitsa, 2/15

Mungathe Kukhalabe ndi Mabwenzi M’dziko Lopanda Chikondi Lino, 10/15

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kutsatira “Khristu”? 5/15

‘Ndinu Mabwenzi Anga,’ 10/15

Olungama Adzatamanda Mulungu Kosatha, 3/15

Pitirizani Kukulitsa Chikondi Chanu Chaubale, 11/15

Sangalalani Ndi Ntchito Yopanga Ophunzira, 1/15

Taonani Mtumiki Amene Yehova Amakondwera Naye, 1/15

Tiyenera Kukhala Aulemu Popeza Ndife Atumiki a Mulungu, 11/15

Tsanzirani Yesu mwa Kulalikira Molimba Mtima, 7/15

Umphumphu Wanu Umakondweretsa Mtima wa Yehova, 4/15

“Yakani ndi Mzimu,” 10/15

Yamikirani Malo Anu Mumpingo wa Mulungu, 11/15

Yang’ananibe pa Mphoto, 3/15

Yehova Ndi Woyenera Kutamandidwa ndi Tonsefe, 3/15

Yesetsani Kukula Mwauzimu Chifukwa “Tsiku Lalikulu la Yehova Lili Pafupi,” 5/15

Yobu Analemekeza Dzina la Yehova, 4/15

Zimene Yesu Anaphunzitsa Zimatithandiza Kukhala Osangalala, 2/15

NKHANI ZOSIYANASIYANA

Abambo a Atumwi, 7/1

Kodi Aisiraeli Ankakhulupirira Nyenyezi? 3/1

Alembi omwe ankatsutsa Yesu, 8/1

Amene Anali ndi Dzina Loti Yakobe, 9/1

“Ameni,” 6/1

“Ana a Zeu” (Mac. 28:11), 3/1

Anachita Zinthu Mwanzeru (Abigayeli), 7/1

Anaphunzira Chifundo (Yona), 4/1

Anaphunzira pa Zolakwa Zake (Yona), 1/1

Anathetsa Mantha ndi Kukayikira (Petulo), 10/1

Anthu Anaukira Mtumwi Paulo Pamene Amalalikira ku Efeso, 2/1

Ayuda ‘Anachita Zinthu Mosadziwa’ (Mac. 3:17), 6/15

“Buku la Yasari” Komanso “Buku la Nkhondo za Yehova,” 3/15

Chaka Chatsopano (Asia), 12/1

Chikhulupiriro Cholimba, 5/1

Chilichonse Chili ndi Nthawi, 3/1

Chipembedzo Chabwino, 8/1

Dzitetezeni ku Mizimu Yoipa, 5/1

Kodi Adamu ndi Hava Anali Anthu Enieni? 9/1

Kodi Aisiraeli Ankachita Ulimi wa Njuchi? 7/1

Kodi Akhristu Ayenera Kumenya Nkhondo? 10/1

Kodi Amishonale Analalikira Kum’mawa Mpaka Kukafika Kuti? 1/1

Kodi Anthu Ankakonda Dzombe? (Mt 3:4), 10/1

Kodi Apezadi Chingalawa cha Nowa? 7/1

Kodi Mdyerekezi Ndi Munthu Weniweni? 10/1

Kodi Mulungu Amapatsa Mphamvu Anthu Onse Ochiritsa Mozizwitsa? 5/1

Kodi Mulungu Analemberatu Zomwe Zidzachitikire Munthu Aliyense? 4/1

Kodi Mumaopa Akufa? 1/1

Kodi Mwapatula Nthawi Yophunzirira Baibulo? 10/15

Kodi N’zotheka Kuyamba Kukhulupirira Mlengi? 10/1

Kodi Satana Anachotsedwa Liti Kumwamba? 5/15

Kodi Zipembedzo Zonse Zimalambira Mulungu Mmodzi? 6/1

Kodi Zochitika Zonse Pamoyo Wanu Zinalembedweratu? 3/1

Kubadwa Mwatsopano, 4/1

Kudzozedwa Kunkatanthauza Chiyani? 8/1

Kulambira Baala ndi Chiwerewere, 11/1

Kulambira kwa Pabanja, 10/15

Kusiyana Maganizo Pankhani ya Mzimu Woyera, 10/1

Kuukitsidwa kwa Lazaro, 3/1

‘Kuzika Mizu ndi Kukhazikika pa Maziko,’ 10/15

Likasa la Chipangano, 9/1

Matenda a Khate M’Baibulo, 2/1

Mayina Atanthauzo, 2/1

Mfumu Davide Ankakonda Kuyimba, 12/1

“Mfumu Herode,” 12/1

Mfundo 6 Zabodza Zimene Akhristu Sayenera Kukhulupirira, 11/1

Mnyamata Wolimba Mtima (Davide), 1/1

Mpanda wa Zisonga Kuzungulira Yerusalemu, 5/1

Mtendere M’dziko la Mavutoli, 7/1

Mtengo ‘Umene Tsamba Lake Silifota,’ 3/1

Mvula, 1/1

Mwana wa Mlongo Wake wa Paulo, 6/1

Mwana Wasukulu Apha Anthu Ambiri, 12/1

Mzinda wa Korinto, 3/1

Ngalande ya Hezekiya, 5/1

Ngati Mwana Wabadwa Wakufa, Angauke? 4/15

Phunziro la pa Miyambo 24:27, 10/15

Pilato Ankaopa Kaisara? 1/1

Rahabi, 8/1

Sanakayikire Malonjezo a Mulungu (Abulahamu), 7/1

Semu, 10/1

“Tidya Chiyani?” 8/1

Urimu ndi Tumimu, 6/1

Usodzi Panyanja ya Galileya, 10/1

“Woyang’anira Kachisi,” 10/1

Yeremiya, 12/1

Yoasi, 4/1

Yosiya, 2/1

Zimene Zinachititsa Kuti Dzikoli Lisakhale Paradaiso, 11/1

Zodabwitsa pa Pentekosite, 9/1

YEHOVA

Akuluakulu a Katolika Akufuna Kusiyiratu Kugwiritsa Ntchito Dzina Lake, 4/1

Amadziwa Zimene Sitingakwanitse, 6/1

Amafuna Kuti Zizitiyendera Bwino, 12/1

Amakonda Anthu Ofatsa, 8/1

Amatipatsa Ufulu Wosankha, 11/1

Anafotokoza Makhalidwe Ake, 5/1

Atate wa Ana Amasiye, 4/1

Athetsa Mavuto Onse? 12/1

Kodi Amafuna Kuti Mukhale Wolemera? 9/1

Kodi Amasintha Maganizo Ake? 6/1

Kodi Amatenga Ana Kuti Akakhale Angelo Kumwamba? 3/1

Kodi Amavomereza Mitala? 7/1

Kodi Mulungu Ndani? 2/1

Kodi Mungamuyandikire mwa Kusala Kudya? 4/1

Kodi Pali Amene Amasamaladi za Ine? 6/1

Kodi Tikamavutika Ndiye Kuti Akutilanga? 6/1

Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizichita Chiyani? 10/1

Kodi Yesu Ndi Mulungu? 2/1, 4/1

Kuopa Mulungu Osati Anthu, 3/1

Musaiwale Yehova, 3/15

Ndi Amene Angapulumutse Dzikoli, 1/1

“Ndidziwa Zowawitsa Zawo” (Eks 3:1-10), 3/1

Umboni Waukulu Wakuti Amatikonda, 2/1

Woweruza Moyenera Nthawi Zonse, 1/1

Woweruza Wachilungamo, 9/1

Woyera, 7/1

Yesu ndi Atate Ake ndi Amodzi? 9/1

YESU KHRISTU

Afarisi Ankafanana ndi “Manda Opaka Laimu Woyera,” 11/1

Anaphunzitsa za “Mapeto,” 5/1

Anaphunzitsa za Moyo wa Banja, 11/1

Anaphunzitsa za Tsogolo la Anthu, 8/1

Anatchula Yehova kuti “Abba, Atate” 4/1

Asilikali Achiroma Anasirira Malaya Ake Amkati, 7/1

Kalembera Amene Anachititsa Kuti Abadwire ku Betelehemu, 12/1

Kodi Anzeru Atatu Anakaona Yesu Ali Mwana? 12/1

Kodi Yesu Ndi Mulungu? 2/1, 4/1

Mapemphero Amene Mulungu Amamva, 2/1

N’chifukwa Chiyani Anasambitsa Mapazi a Atumwi Ake? 1/1

Sanagonje Poyesedwa, 5/1

Yesu ndi Atate Ake ndi Amodzi? 9/1

Yosefe Anaganiza Zopatsa Mariya Kalata Yothetsera Ukwati, 12/1