Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozerankhani Wa Nkhani Za M’magazini A Nsanja Ya Olonda A 2004

Mlozerankhani Wa Nkhani Za M’magazini A Nsanja Ya Olonda A 2004

 Mlozerankhani Wa Nkhani Za M’magazini A Nsanja Ya Olonda A 2004

Wosonyeza deti la magazini yopezekamo nkhaniyo

BAIBULO

‘Anayendayenda Kufalitsa Uthenga Wabwino’ (G. Borrow), 8/15

Chuma cha Chester, 9/15

Complutensian Polyglot, 4/15

“Lomasuliridwa Bwino Kwambiri” (New World Translation), 12/1

Mfundo Zazikulu za M’buku la Genesis​—I, 1/1

Mfundo Zazikulu za M’buku la Genesis​—II, 1/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Eksodo, 3/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Levitiko, 5/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Numeri, 8/1

Mfundo Zazikulu za M’buku la Deuteronomo, 9/15

Mfundo Zazikulu za M’buku la Yoswa, 12/1

KALENDALA

Chuma Chochuluka cha M’nyanja, 9/15

Malimwe ndi Dzinja Sizidzatha, 7/15

“Mitengo ya Mulungu Yadzala ndi Madzi,” 1/15

‘Mitsinje Iombe M’manja,’ 5/15

“Ntchito Zanu Zichulukadi!” 11/15

‘Wamkulu Kuposa Mapiri,’ 3/15

MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA

Aisrayeli amene anaphedwa anali 23,000 kapena 24,000? (1Akor. 10:8; Num. 25:9), 4/1

Chifukwa chake amuna achiisrayeli ankaloledwa kukwatira akazi amene anawagwira ukapolo, 9/15

Chifukwa chake Yesu analola Tomasi kum’khudza pamene analetsa Mary wa Magadala kutero, 12/1

Hanameli anagulitsa bwanji munda kwa Yeremiya? (Yer. 32:7), 3/1

‘Kongoletsani osayembekeza kanthu konse’ (Luka 6:35), 10/15

Kususuka, 11/1

Nambala ya 144,000 ndi yeniyeni? 9/1

N’chifukwa chiyani Mikala anali ndi terafi? (1Sam. 19:13), 6/1

N’chifukwa chiyani Yuda anagona ndi mkazi amene ankamuyesa wadama? (Gen. 38:15), 1/15

N’chiyani chinachitika ndipo ndani akanaphedwayo? (Eks. 4:24-26), 3/15

Ngalawa imene Paulo anakwera inaswekera ku Melita? 8/15

Ngamila ndi singano zenizeni? (Mat. 19:24; Mk. 10:25; Luka 18:25), 5/15

Njiwa inakatenga kuti tsamba la azitona? (Gen. 8:11), 2/15

‘Osakhulupirira’ (2 Akor. 6:14), 7/1

‘Satana analinkugwa kuchokera kumwamba’ (Luka 10:18), 8/1

Tingamvetse chisoni motani mzimu woyera? (Aef. 4:30), 5/15

Tizigawo tating’ono totengedwa m’magazi, 6/15

Zimene Chaka Choliza Lipenga chimasonyeza za m’tsogolo, 7/15

Ziwanda pa nthawi ya Zaka 1,000, 11/15

MBIRI YA MOYO WANGA

Kuchoka M’ndende Zamdima Kupita ku Mapiri a ku Switzerland (L. Walther), 6/1

Kudalira Chisamaliro cha Yehova (A. Denz Turpin), 12/1

Kukhala Wokhutira ndi Zimene Mulungu Wandipatsa Kwandithandiza (I. Osueke), 3/1

Kusankha Ulamuliro wa Mulungu Mosasunthika (M. Žobrák), 11/1

Maphunziro Amene Ndikupitirizabe Mpaka Pano (H. Gluyas), 10/1

Maso Anatseguka Ngakhale Kuti Ndinali Wakhungu! (E. Hauser), 5/1

Moyo Wanga Wosangalatsa Ngakhale Ndakumana N’zachisoni (A. Hyde), 7/1

Pamoyo Wathu Takhala Tikudalira Mphamvu za Yehova (E. Haffner), 8/1

Tadalitsidwa Chifukwa Chodzimana (G. Aljian), 4/1

Tadalitsidwa Kwambiri Chifukwa Chokhala ndi Mtima Waumishonale (T. Cooke), 1/1

Takhala ndi Moyo Watanthauzo Chifukwa Chodzipereka (M. and R. Szumiga), 9/1

Yehova Anandikomera Mtima (F. King), 2/1

MBONI ZA YEHOVA

‘Anatiphunzitsa Kulemekeza Chipembedzo Chake’ (Italy), 6/15

Anauzako Anthu Am’kalasi Zimene Amakhulupirira (Poland), 10/1

Chikukula, 3/1

Chikumbumtima Chokoma (anabweza telefoni ya m’manja), 2/1

Kalata Yochokera kwa Alejandra (Mexico), 10/1

Kuchita Chokoma Panthaŵi ya Mavuto, 6/1

Kudalitsidwa Chifukwa Chopatsa (zopereka), 11/1

Kukumbukira “Anthu Oiwalika Amene Anazunzidwa,” 9/1

Kulalikira Anthu ku Ntchito, 4/1

Kulalikira Mwamwayi M’gawo la Chingelezi ku Mexico, 4/15

Kusonkhana pa ‘Mchombo wa Dziko’ (Chilumba cha Easter), 2/15

Liberia, 4/1

Misonkhano Yachigawo Yakuti “Patsani Mulungu Ulemerero,” 1/15

Misonkhano Yachigawo Yakuti “Yendani ndi Mulungu,” 3/1

‘Muwolokere Kuno Mudzathangate’ (Bolivia), 6/1

Mwambo Womaliza Maphunziro a Gileadi, 6/15, 12/15

Okhulupirika Ndiponso Osasunthika (Poland), 10/15

Olankhula Zinenero Zamakolo ku Mexico, 8/15

Si Maseŵera Chabe (ana), 10/1

Zisumbu za Tonga, 12/15

MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU

Abrahamu ndi Sara Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo! 5/15

Achinyamata Lolani Kuti Makolo Akuthandizeni Kuteteza Mtima! 10/15

Chitonthozo kwa Ovutika, 2/15

‘Hema wa Oongoka Mtima Adzakula’ (Miy. 14), 11/15

Kudikira M’njira Yoyenera, 10/1

Kukonzera Ana Cholowa, 9/1

Kulimbana ndi Kutaya Mtima, 9/1

Kulimbana ndi Vuto la Kusatsimikizika kwa Zinthu, 2/1

Kuphunzitsa Ana, 6/15

Kusaloŵerera M’ndale Kumalepheretsa Kusonyeza Chikondi? 5/1

Kuyang’ana pa Mphoto, 4/1

‘Limba Nayoni Nkhondo Yabwino ya Chikhulupiriro,’ 2/15

Mavuto Amalamulira Moyo Wanu? 6/1

Mgonero wa Ambuye, 3/15

Mmene Timasonyezera Kuti Timakonda Mulungu, 3/1

Mungatani Kuti Mudziwe Choyenerera ndi Chosayenerera? 12/1

‘Wochenjera Amachita Mwanzeru’ (Miy. 13), 7/15

Zolinga Zauzimu, 7/15

NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA

Achinyamata, Kodi Mukukonzekera Tsogolo? 5/1

“Ambuye, Tiphunzitseni Ife Kupemphera” (Pemphero Lachitsanzo), 2/1

Anthu a Yehova Ayenera Kukonda Khalidwe la Kukoma Mtima, 4/15

Anthu Onse Alengeze Ulemerero wa Yehova, 1/1

‘Aphunzitseni Kusunga Zinthu Zonse Zimene Ndinakulamulirani,’ 7/1

Atumiki Achimwemwe a Yehova, 11/1

Chenjerani ndi “Mawu a Alendo,” 9/1

Chikondi Chokhulupirika cha Yehova N’chachikulu, 1/15

Chilengedwe Chimalengeza Ulemerero wa Mulungu! 6/1

‘Chitani Ntchito ya Mlaliki wa Uthenga Wabwino,’ 3/15

Dalirani Mzimu wa Mulungu Zinthu Zikasintha pa Moyo Wanu, 4/1

Funafunani Yehova, Amene Amayesa Mitima, 11/15

Kanizani Mzimu wa Dziko Lomwe Likusinthali, 4/1

“Kapolo” Amene Ali Wokhulupirika ndi Wanzeru, 3/1

“Kapolo Wokhulupirika” Wapambana Mayeso! 3/1

Khalani ndi Maganizo a Kristu Pankhani ya Kukhala Wamkulu, 8/1

Khalanibe Odzisunga mwa Kutchinjiriza Mtima Wanu, 2/15

Khalani Wolimba Mtima Ngati Yeremiya, 5/1

Kukhala Okoma Mtima M’dziko Losaganiziranali, 4/15

Kusamalira Okalamba Ndi Udindo wa Akristu, 5/15

‘Kwaniritsani Utumiki Wanu,’ 3/15

Lankhulani Mawu a Mulungu Molimba Mtima, 11/15

Lemekezani Mulungu ndi ‘Pakamwa Pamodzi,’ 9/1

“Liwu Lawo Linatulukira ku Dziko Lonse Lapansi,” 1/1

‘Maonekedwe a Dzikoli Akusintha,’ 2/1

Mowa Umafunika Kusamala Nawo, 12/1

“Mukani, Phunzitsani,” 7/1

“Mukondane ndi Chikondi Chaubale,” 10/1

Muli ndi Chifukwa Chomveka Choyembekezera Paradaiso? 10/15

Mumakondwera ndi ‘Chilamulo cha Yehova’? 7/15

Mumalola Kuti Yehova Akuthandizeni? 12/15

Ndani Amene Akupatsa Mulungu Ulemerero Masiku Ano? 10/1

Odala Ndi Amene Amapatsa Mulungu Ulemerero, 6/1

Odedwa Popanda Chifukwa, 8/15

Okalamba Ndi Ofunika Kwambiri pa Ubale Wathu Wachikristu, 5/15

Onani Mphatso ya Moyo Wanu Kuti Ndi Yamtengo Wapatali, 6/15

Otopa Koma Osalefuka, 8/15

Ozunzidwa Komabe Achimwemwe, 11/1

Peŵani Chinyengo, 2/15

“Tadzilimbikani mwa Ambuye,” 9/15

Tonthozanani, 5/1

Tsatirani Malangizo a Mulungu Wamoyo, 6/15

Ukulu wa Yehova Ndi Wosasanthulika, 1/15

Yehova Adzaweruza Oipa, 11/15

Yehova Amaonetsa Ulemerero Wake kwa Odzichepetsa, 8/1

Yehova Amatipatsa Zimene Timafunikira Tsiku Lililonse (Pemphero Lachitsanzo), 2/1

Yehova Ndiye ‘Linga Lathu M’nyengo ya Nsautso,’ 8/15

Yehova Ndiye Mthandizi Wathu, 12/15

Yendani mu Umphumphu, 12/1

‘Yendayenda M’dzikoli,’ 10/15

“Zida Zonse za Mulungu,” 9/15

‘Zimene Yehova Watsimikiza’ Sizingalephereke, 7/15

NKHANI ZOSIYANASIYANA

666​—Si Nambala Yongodabwitsa Chabe, 4/1

“Anapita M’ngalawa ku Kupro,” 7/1

Atsogoleri a Zipembedzo Aziloŵerera M’ndale? 5/1

Atumiki a Mulungu Ali Ngati Mitengo, 3/1

Boma Labwino, 8/1

Boma la Ufumu Likuchita Zooneka, 8/1

Chilombo ndi Chizindikiro Chake, 4/1

Chimwemwe, 9/1

Chipembedzo Ndicho Chikuchititsa Mavuto? 2/15

Ehudi, 3/15

Gulu la Anabaptist, 6/15

“Imodzi Mwa Ntchito Zimene Panagona Luso Kwambiri” (Thaŵale Lamkuwa), 1/15

Kalata Yopita kwa Nowa, 7/1

Kapadokiya, 7/15

Kukonda Zinthu Zauzimu Kumakhudza Moyo, 2/1

Kulambira Koona ndi Uchikunja Zinalimbana (Efeso), 12/15

Kupeza Malangizo Abwino, 8/15

Mapemphero Angasinthitse Zinthu? 6/15

Maseŵera Akale, 5/1

Matchalitchi Apulumuka Mavuto Awo? 3/1

“Mulungu Woona ndi Moyo Wosatha” (1 Yoh. 5:20), 10/15

Mumafuna Kukhala ndi Moyo Wosatha? 11/15

Mungadalire Malonjezo a Ndani? 1/15

Muyenera Kukhala M’chipembedzo Chinachake? 6/1

N’chiyani Chimapangitsa Moyo Kukhala ndi Cholinga Chenicheni? 8/1

“Ofatsa Choloŵa Chawo ndi Dziko Lapansi,” 10/1

Pangano la Mtendere la ku Westphalia, 3/15

Pemphero la Ambuye, 9/15

Rebeka, 4/15

Tingayembekezere Mtendere, 1/1

Tiyenera Kupemphera kwa Angelo Kuti Atithandize? 4/1

Utsogoleri Wabwino, 11/1

Zinthu Zauzimu, 10/15

Zinthu Zauzimu Zimene Mumafunikira, 2/1

Zogayira Chakudya Chathu, 9/15

YEHOVA

Amakuganizirani, 7/1

Amatiganizira? 1/1

Kudzichepetsa, 11/1

‘Kufuna Kwanu Kuchitidwe Pansi Pano,’ 4/15

Kukondweretsa Mulungu? 5/15

“Ntchito Zanu Zichulukadi!” 11/15

YESU KRISTU

Kubadwa Kwake N’koyenera Kukukumbukira, 12/15

Zozizwitsa Zinali Zenizeni Kapena Nthano Chabe? 7/15