NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) September 2024

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira November 11–​December 8, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 36

“Muzichita Zimene Mawu Amanena”

Idzaphunziridwa mlungu woyambira November 11-17, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 37

Kalata Imene Ingatithandize Kupirira Mokhulupirika Mpaka Mapeto

Idzaphunziridwa mlungu woyambira November 18-24, 2024.

MBIRI YA MOYO WANGA

Moyo Wabwino Kwambiri Potumikira Yehova

André Ramseyer wakhala mu utumiki wa nthawi zonse kwa zaka 70 ndipo wakhala akugwira ntchito zosiyanasiyana. Kodi ndi mavuto ati amene anakumana nawo, nanga wasonyeza bwanji kuti amaika Yehova pamalo oyamba?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi ophunzira 70 omwe Yesu anawatuma kukalalikira aja, anali kuti pomwe iye ankayambitsa mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye? Kodi anali atamusiya?

NKHANI YOPHUNZIRA 38

Kodi Mumamvera Machenjezo?

Idzaphunziridwa mlungu wa November 25–​December 1, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 39

Kupatsa Kumatichititsa Kukhala Osangalala

Idzaphunziridwa mlungu woyambira December 2-8, 2024.

Muzikhala Okonzeka Kuphunzira Zinthu Zatsopano

Kodi tingatani kuti pophunzira patokha tizimvetsa zimene Yehova akutiphunzitsa?