NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) September 2022

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira November 7–December 4, 2022.

NKHANI YOPHUNZIRA 37

Muzikhulupirira Abale Anu

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi ndi anthu ati omwe adzaukitsidwire padzikoli, nanga kuuka kwake kudzakhala kotani?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi mtumwi Paulo ankatanthauza chiyani pomwe anadzitchula kuti anali ngati “khanda lobadwa masiku asanakwane”? (1 Akorinto 15:8)

MBIRI YA MOYO WANGA

Ndakhala Ndikusangalala Kuphunzira Komanso Kuphunzitsa Zokhudza Yehova

Mbiri ya Moyo Wanga: Leon Weaver, Jr.