NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) September 2016

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira October 24 mpaka November 27, 2016.

Manja Anu ‘Asalefuke’

Kodi Yehova amalimbikitsa bwanji atumiki ake? Nanga ifeyo tingamutsanzire bwanji?

Pitirizani Kulimbana ndi Zimene Zingakulepheretseni Kupeza Madalitso

Anthu a Mulungu amakumana ndi mavuto ambiri pamene akuyesetsa kuti iye azisangalala nawo. Komabe akhoza kupambana

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Lemba la Aheberi 4:12 limati “mawu a Mulungu ndi amoyo ndi amphamvu” Kodi mawu amene akutchulidwa palembali ndi ati?

Paulo Anateteza Uthenga Wabwino kwa Akuluakulu a Boma

Tingaphunzire zambiri kwa Paulo tikaganizira mmene ankagwiritsira ntchito malamulo a boma podziteteza komanso poteteza uthenga wabwino.

Kodi Mavalidwe Anu Amalemekeza Mulungu?

Mfundo za m’Malemba zingatithandize kudziwa zovala zoyenera.

Muzilola Kuti Yehova Azikutsogolerani

A Mboni a ku Poland ndi ku Fiji anasankha bwino.

Achinyamata, Yesetsani Kulimbitsa Chikhulupiriro Chanu

Kodi nthawi zina mumaona kuti ndi bwino kutsatira zimene anthu ambiri amakhulupirira, monga zoti zinthu zinachita kusintha osati kulengedwa? Ngati ndi choncho, mfundo za m’nkhaniyi zikuthandizani.

Muzithandiza Ana Anu Kuti Akhale Ndi Chikhulupiriro Cholimba

Kodi mumaona kuti simungakwanitse kuphunzitsa bwinobwino ana anu? Onani mfundo 4 zimene zingakuthandizeni.