NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) November 2023

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira January 8–February 4, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 46

Mmene Yehova Anatsimikizira Lonjezo Lake la Paradaiso

Idzaphunziridwa mlungu woyambira January 8-14, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 47

Kodi Tingatani Kuti Tizikondana Kwambiri?

Idzaphunziridwa mlungu woyambira January 15-21, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 48

Mukhoza Kukhalabe Olimba Mtima pa Nthawi Yovuta

Idzaphunziridwa mlungu woyambira January 22-28, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 49

Kodi Yehova Amayankha Mapemphero Anga?

Idzaphunziridwa mlungu woyambira January 29–​February 4, 2024.

MBIRI YA MOYO WANGA

Ndimakhala Wosatekeseka Chifukwa Chodalira Yehova

Mbiri ya moyo wanga: Israel Itajobi.

Hulda Anakwaniritsa Cholinga Chake

Kodi Hulda anatani kuti apeze tabuleti yoti izimuthandiza mu utumiki komanso pamisonkhano?