NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) March 2016

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa May 2 mpaka pa May 29, 2016.

Achinyamata, Kodi Ndinu Okonzeka Kubatizidwa?

Mafunso atatu amene angakuthandizeni kusankha bwino zochita pa nkhaniyi.

Achinyamata, Kodi Mungakonzekere Bwanji Kubatizidwa?

Mungatani ngati mukuona kuti simunakonzeke? Nanga mungatani ngati mukufuna kubatizidwa koma makolo anu akuti mudikire kaye?

Kodi Tingathandize Bwanji Kulimbitsa Mgwirizano Wathu?

Masomphenya opezeka mu Chivumbulutso chaputala 9 amasonyeza kuti mgwirizano ndi wofunika.

Yehova Amatsogolera Anthu Ake Kuti Adzapeze Moyo

Tingasonyeze bwanji kuti timafuna kuti Yehova azititsogolera?

Kodi Mungathandize Bwanji Mpingo Wanu?

Mukhoza kukhala mmishonale mumpingo wanu.

Muzitsanzira Aneneri

Zitsanzo za aneneri monga Ezekieli, Yeremiya ndi Hoseya zingatithandize tikatopa, tikakhumudwa komanso tikapatsidwa ntchito yovuta.

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi anthu a Mulungu analowa liti mu ukapolo wa m’Babulo Wamkulu? Kodi Satana anapitadi ndi Yesu kukachisi kapena anangomuonetsa masomphenya?