NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) June 2016

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira August 1 mpaka 28, 2016.

Yehova “Amakuderani Nkhawa”

Werengani nkhaniyi kuti muone umboni woti Mulungu amakuganizirani

Tiziyamikira Kuti Yehova Amatiumba

Kodi Yehova amasankha bwanji anthu oti awaumbe? N’chifukwa chiyani amawaumba? Nanga amawaumba bwanji?

Kodi Mumalola Kuti Yehova Azikuumbani?

Kodi ndi makhalidwe ati amene angakuthandizeni kuti Mulungu akuumbeni mosavuta?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi munthu wokhala ndi kachikwama ka mlembi komanso amuna 6 onyamula zida zophwanyira otchulidwa m’masomphenya a Ezekieli akuimira ndani?

“Yehova Mulungu Wathu Ndi Yehova Mmodzi”

Kodi mawu akuti Yehova Mulungu ndi “mmodzi” amatanthauza chiyani ndipo tingatani kuti tizimulambira mogwirizana?

Tisasiye Kutumikira Mulungu Chifukwa cha Zochita za Ena

Nawonso atumiki okhulupirika akale nthawi zina ankalankhula komanso kuchita zinthu zimene zinkakhumudwitsa ena. Kodi tikuphunzirapo chiyani pa zitsanzo za m’Baibulo zimenezi?

Khalidwe la Mtengo Wapatali Kuposa Dayamondi

Tiyenera kuyesetsa kuti tikhale ndi khalidwe limeneli.

Kodi Mukukumbukira?

Kodi mwawerenga magazini aposachedwapa a Nsanja ya Olonda? Onani zimene mungathe kukumbukira.