Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2017

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2017

Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo

BAIBULO

 • Elias Hutter Anamasulira Mabaibulo, Na. 4

 • Kusamvetsa, Na. 1

 • Kuwerenga Kuzikusangalatsani, Na. 1

 • N’chifukwa Chiyani Pali Osiyanasiyana? Na. 6

 • Umboni Wina Wosonyeza Kuti Ndi Lolondola (Tattenai anali munthu weniweni), Na. 3

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

 • Ndinkakonda Kwambiri Masewera a Baseball Kuposa Chilichonse (S. Hamilton), Na. 3

 • Ndinkaona Kuti Kulibe Mulungu (A. Golec), Na. 5

 • Sindinkafuna Kufa (Y. Quarrie), Na. 1

MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA

 • Kodi Akhristu angagwiritse ntchito lupu (IUD) ngati njira ya kulera? Dec.

 • Kodi mwana woyamba kubadwa ndi amene ankakhala mumzere wa makolo a Mesiya? Dec.

 • Kodi ndi nzeru kuti Mkhristu azisunga mfuti pofuna kudziteteza kwa anthu? July

 • N’chifukwa chiyani nkhani zokhudza moyo wa Yesu ali mwana zimene Mateyu ndi Luka analemba zimasiyana? Aug.

 • Yehova “sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapirire” (1Akor. 10:13), Feb.

MBIRI YA MOYO

 • Kuyenda ndi Anthu Anzeru Kwandithandiza Kwambiri (W. Samuelson), Mar.

 • Mulungu Anatisonyeza Kukoma Mtima Kwakukulu M’njira Zambiri (D. Guest), Feb.

 • Ndakhala ndi Mwayi Wotumikira Limodzi ndi Abale Okhulupirika (D. Sinclair), Sept.

 • Ndinasiya Zinthu Zambiri Kuti Nditsatire Ambuye (F. Fajardo), Dec.

 • Ndine Msilikali wa Khristu (D. Psarras), Apr.

 • Tikapirira Mavuto Tidzadalitsidwa (P. Sivulsky), Aug.

 • Timadalitsidwa Tikamachita Zimene Yehova Amatiuza (O. Matthews), Oct.

 • Vuto Losamva Silinandilepheretse Kuphunzitsa Anthu Ena Baibulo (W. Markin), May

MBONI ZA YEHOVA

 • Anadzipereka ndi Mtima Wonse (alongo osakwatiwa), Jan.

 • Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Turkey, July

 • Anamusonyeza Kukoma Mtima, Oct.

 • Kodi Mungatani Kuti Muzolowere Mpingo Wanu Watsopano? Nov.

 • “Kodi Tichitanso Liti Msonkhano Wina?” (Mexico), Aug.

 • ‘Kukonda Kwambiri Yehova Ndiponso Kulalikira Mwakhama’ (msonkhano wa 1922), May

 • “Kungatalike Bwanji Ndipo Msewu Ungaipe Bwanji Ankafikako” (Australia), Feb.

 • Moyo Wosalira Zambiri Ndi Wosangalatsa, May

 • “Munthu Wopatsa Adzadalitsidwa” (zopereka), Nov.

MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU

 • Chikondi Ndi Khalidwe Lamtengo Wapatali Kwambiri, Aug.

 • Kodi Akhristu Ayenera Kukondwerera Khirisimasi? Na. 6

 • Kodi Atumiki Achikhristu Safunika Kukwatira? Na. 2

 • Kodi Mumakhalabe Bwenzi Labwino Zinthu Zikavuta? Mar.

 • Kodi Mumathetsa Kusamvana N’kukhazikitsa Mtendere? June

 • Kodi Tizitani Tikalakwitsa Zinthu? Na. 6

 • Tetezani Maganizo Anu, July

 • Ubwino wa Mtima Wopatsa, Na. 2

NKHANI ZOPHUNZIRA

 • Achinyamata “Pitirizani Kukonza Chipulumutso Chanu,” Dec.

 • Cholinga cha Yehova Chidzakwaniritsidwa, Feb.

 • Choonadi Sichibweretsa “Mtendere Koma Lupanga,” Oct.

 • Dipo Ndi ‘Mphatso Yangwiro’ Yochokera kwa Atate, Feb.

 • “Khulupirira Yehova Ndipo Chita Zabwino,” Jan.

 • Kodi Masomphenya a Zekariya Akukukhudzani Bwanji? Oct.

 • Kodi Mukhoza Kuyembekezera Moleza Mtima? Aug.

 • Kodi Mumathawira kwa Yehova? Nov.

 • Kodi Mumatsanzira Yehova pa Nkhani ya Chilungamo? Apr.

 • Kodi Mumatsatira Ndi Mtima Wonse Zimene Zinalembedwa? Mar.

 • Kodi Ndi Ndani Akutsogolera Anthu a Mulungu Masiku Ano? Feb.

 • Kodi Tingatani Kuti Nthawi Zonse Tizikhala Odzichepetsa? Jan.

 • Kodi Tingathandize Bwanji Ana a Anthu Ochokera M’mayiko Ena? May

 • Kodi Ufumu wa Mulungu Ukadzabwera Udzachotsa Zinthu Ziti? Apr.

 • “Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?” May

 • Kudzichepetsa N’kofunika Kwambiri, Jan.

 • Kudzipereka Kwathu Kumachititsa Kuti Yehova Atamandidwe, Apr.

 • ‘Limba Mtima Ndipo Ugwire Ntchitoyi,’ Sept.

 • “Lirani ndi Anthu Amene Akulira,” July

 • ‘Mawu a Mulungu Ndi Amphamvu,’ Sept.

 • “Mawu a Mulungu Wathu Adzakhala Mpaka Kalekale,” Sept.

 • ‘Mtendere wa Mulungu Umaposa Kuganiza Mozama Kulikonse,’ Aug.

 • ‘Mulungu Akwaniritse Zofuna Zanu,’ July

 • Musalole Kuti Chikondi Chanu Chizirale, May

 • Musalole Kuti Chilichonse Chikulepheretseni Kulandira Mphoto, Nov.

 • Musamaiwale Nkhani Yofunika Kwambiri, June

 • Muzifunafuna Chuma Chenicheni, July

 • Muzikhala Kumbali ya Ulamuliro wa Yehova, June

 • Muzikhulupirira Yehova Kuti Muzisankha Zochita Mwanzeru, Mar.

 • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kutamanda Yehova? July

 • “Ndikudziwa Kuti Adzauka,” Dec.

 • “Ndili ndi Chiyembekezo mwa Mulungu,” Dec.

 • Pewani Kutengera Maganizo a M’dzikoli, Nov.

 • Thandizani Ana Anu Kupeza Nzeru Kuti Adzapulumuke, Dec.

 • Timatetezedwa ndi Magaleta Komanso Chisoti Chachifumu, Oct.

 • Tiziimba Mosangalala, Nov.

 • Tizikonda ndi Mtima Wonse Chuma Chimene Mulungu Watipatsa, June

 • Tizipereka Ulemu kwa Oyenera Kulemekezedwa, Mar.

 • “Tizisonyezana Chikondi Chenicheni M’zochita Zathu,” Oct.

 • Tizithandiza Alendo Kuti ‘Azitumikira Yehova Mokondwera,’ May

 • Tizitsanzira Yehova pa Nkhani ya Chifundo, Sept.

 • Tizitumikira Yehova ndi Mtima Wathunthu, Mar.

 • Tiziyesetsa Kukhala Odziletsa, Sept.

 • Tsanzirani Chilungamo ndi Chifundo cha Yehova, Nov.

 • Ufulu Wosankha Zochita Ndi Mphatso Yapadera, Jan.

 • “Uzikwaniritsa Zinthu Zimene Walonjeza,” Apr.

 • Valani Umunthu Watsopano Ndipo Musauvulenso, Aug.

 • “Woweruza wa Dziko Lonse Lapansi” Amachita Zachilungamo, Apr.

 • Yehova Amatitonthoza M’masautso Athu Onse, June

 • Yehova Amatsogolera Anthu Ake, Feb.

 • Zimene Zinawathandiza Kuvula Umunthu Wakale, Aug.

 • ‘Zinthu Zimenezo Uziziphunzitsa kwa Anthu Okhulupirika,’ Jan.

NKHANI ZOSIYANASIYANA

 • Akapolo Anapeza Ufulu, Na. 2

 • Anthu 4 Okwera Pamahatchi, Na. 3

 • Dzina la M’Baibulo Pamtsuko Wakale, Mar.

 • Kachilembo Kachiheberi, Na. 4

 • Kodi Amalonda Amene Ankagulitsa Nyama Kukachisi Analidi Ngati “Achifwamba?” June

 • Kodi Angelo Angakuthandizeni? Na. 5

 • Kodi Ayuda Anali ndi Chizolowezi Chotani Chomwe Chinachititsa Yesu Kuuza Anthu Kuti Asamalumbire? Oct.

 • Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Imfa? Na. 4

 • Kodi Dzikoli Lidzakhaladi Paradaiso Kapena Ndi Maloto Chabe? Na. 4

 • Kodi Gayo Ankathandiza Bwanji Akhristu Anzake? May

 • Kodi Kale Anthu Ankanyamula Bwanji Moto? Jan.

 • Kodi Padzikoli Padzakhaladi Mtendere? Na. 5

 • Kodi Tili ‘M’masiku Otsiriza’? Na. 2

 • Kuvutika, Na. 1

 • Malangizo Amene Paulo Anapereka Okhudza Ulendo (Mac. 27), Na. 5

 • Mphatso Yamtengo Wapatali Kuposa Zonse, Na. 6

 • ‘Mulungu Anakondwera Naye’ (Inoki), Na. 1

 • Mungatani Ngati Munthu Amene Mumamukonda Akudwala Matenda Oti Sachira? Na. 4

 • “Ndiwe Mkazi Wokongola” (Sara), Na. 3

 • Nkhawa, Na. 4

 • Tisamaweruze Anthu Chifukwa cha Maonekedwe Awo, June

 • “Udalitsike Chifukwa cha Kulingalira Bwino Kwako” (Abigayeli), June

 • Yehova Anamutchula Kuti “Mfumukazi” (Sara), Na. 5

 • Yosefe wa ku Arimateya, Oct.

YEHOVA

 • Amachititsa Kuti Tizivutika? Na. 1

 • Mulandira Mphatso Yaikulu Imene Mulungu Wapereka? Na. 2

YESU KHRISTU

 • Kodi fanizo la Yesu la “tiagalu” linali lonyoza? Na. 5

 • Kodi Yesu Ankaoneka Bwanji? Na. 6