Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mawu Oyamba

Mawu Oyamba

KODI INUYO MUKUGANIZA BWANJI?

Kodi ndi ndani amene anatipatsa mphatso yabwino kwambiri kuposa zonse?

Baibulo limati: “Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba, pakuti imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zonse zakuthambo.”​Yakobo 1:17.

Nsanja ya Olonda iyi ikutithandiza kudziwa mphatso imene Mulungu watipatsa yomwe ndi yaikulu kuposa mphatso zonse.