Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA Na. 3 2021 | Kodi Mungatani Kuti Mukhale Ndi Tsogolo Labwino?

Kodi mungatani kuti mukhale ndi tsogolo labwino? M’magaziniyi muona zinthu zosiyanasiyana zimene anthu ena amachita pofuna kukhala ndi tsogolo labwino. Muonanso kumene mungapeze malangizo odalirika omwe angakuthandizeni kuti mukhaledi ndi tsogolo labwino.

 

Aliyense Amafuna Kukhala Ndi Tsogolo Labwino

Kodi muyenera kudalira malangizo a ndani m’dziko mukachitika mavuto omwe simunkawayembekezera?

Kodi Tsogolo Lanu Mungalidziwe Bwanji?

Anthu ambiri amene amakhulupirira kuti munthu akamwalira amakabadwanso kwinakwake, okhulupirira nyenyezi, feng shui komanso amene amalambira mizimu yamakolo, amaganiza kuti pali mphamvu zinazake zosaoneka zomwe zingawathandize kudziwa zokhudza tsogolo lawo.

Kodi Maphunziro Ndi Ndalama Zingatithandize Kukhala Ndi Tsogolo Labwino?

Anthu ambiri aona kuti maphunziro akuyunivesite ndiponso chuma sizinawathandize kupeza zomwe ankayembekezera.

Kodi Kungokhala Munthu Wabwino N’kumene Kungachititse Kuti Tikhale Ndi Tsogolo Labwino?

Kukhala munthu wabwino ndi kofunika kwambiri. Komabe, sizitanthauza kuti munthu sungakumane ndi mavuto.

Kodi Malangizo Odalirika Okhudza Tsogolo Labwino Tingawapeze Kuti?

Tikamafuna kusankha zochita pa nkhani inayake, nthawi zambiri timafunsira nzeru kwa munthu wamkulu komanso wanzeru kuposa ifeyo. Mofananamo, n’zotheka kupeza malangizo odalirika okhudza tsogolo lathu.

Zomwe Mungasankhe Zingakhudze Tsogolo Lanu

Kodi tingasankhe zinthu ziti pa moyo wathu?

N’zotheka Kukhala Ndi Tsogolo Labwino

Kodi mukuganiza kuti n’chiyani chingakuthandizeni kuti mukhale ndi tsogolo labwino?