Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

“Amakuderani Nkhawa”

“Amakuderani Nkhawa”

Ngakhale anthu ena atakukhumudwitsani, pali wina amene sangakukhumudwitseni. Kodi ameneyu ndi ndani?

Mfumu Davide ananena kuti: “Ngakhale bambo anga ndi mayi anga atandisiya, Yehova adzanditenga.”​—Salimo 27:10.

Yehova ndi “Tate wachifundo chachikulu ndi Mulungu amene amatitonthoza m’njira iliyonse, amenenso amatitonthoza m’masautso athu onse.”​—2 Akorinto 1:3, 4.

“Muzimutulira nkhawa zanu zonse, pakuti amakuderani nkhawa.”​—1 Petulo 5:7.

Kuti mudziwe mmene Mulungu angakuthandizireni, werengani mutu 12 m’buku lakuti, Zimene Baibulo Limaphunzitsa. Bukuli ndi lofalitsidwa ndi a Mboni za Yehova ndipo likupezekanso pa www.jw.org/ny