Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mawu Oyamba

Mawu Oyamba

Kodi M’tsogolomu Muli Zotani?

Kodi munayamba mwadzifunsapo kuti tsogolo lanu komanso la banja lanu lidzakhala lotani? Baibulo limati:

“Olungama adzalandira dziko lapansi, ndipo adzakhala mmenemo kwamuyaya.”​—Salimo 37:29.

Nsanja ya Olonda iyi ikuthandizani kudziwa cholinga cha Mulungu kwa anthu komanso dzikoli. Ikufotokozanso zimene mungachite kuti mudzasangalale cholingachi chikadzakwaniritsidwa.