NSANJA YA OLONDA Na. 1 2016 | N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuchita Zinthu Moona Mtima?

Anthu ambiri amanama kamodzi akamacheza ndi anzawo pa 10 minitsi iliyonse. Popeza anthu ambiri amanama, palinso chifukwa chosiyira kunena bodza?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Kukhala Oona Mtima N’kwachikale?

Zimene zinachitikira a Hitoshi zingachititse anthu ena kuona kuti kukhala oona mtima n’kwachikaledi.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Chinyengo N’choopsa Bwanji?

Dziwani zoona zokhudza kunena bodza.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Ubwino Wopewa Chinyengo Ndi Wotani?

Zimene zinachitikira anthu ena zikusonyeza kuti kupewa chinyengo n’kothandiza kwambiri.

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Ndithandizeni Kuti Ndikhaleko Mosangalala Komanso Mwamtendere kwa Chaka Chimodzi Chokha

Lemba la 1 Yohane 1:9, linamuthandiza kwambiri Alain Broggio.

Kodi Mukudziwa?

mipukutu inkapangidwa bwanji, nanga ankaigwiritsa ntchito bwanji? Kodi “ansembe aakulu” omwe amatchulidwa m’Malemba Achigiriki Achikhristu anali ndani?

N’chiyani Chingakuthandizeni Kuti Musamakhale Mwamantha?

Mfundo zitatu zothandiza kuti musamadzione ngati wosafunika.

MFUNDO ZAKALE KOMA ZOTHANDIZA MASIKU ANO

Musamade Nkhawa

Yesu ananena kuti tisamade nkhawa ndipo anafotokozanso zimene tingachite kuti tisamade nkhawa.

Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Kodi anthu amene anamwalira adzakhalanso ndi moyo?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Baibulo Lingandithandize Ngati Ndili ndi Nkhawa?

Pali zinthu zitatu zimene Mulungu amapereka kuti athandize anthu amene ali ndi nkhawa.