NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) February 2019

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira April 8 mpaka May 5, 2019

Pitirizani Kukhala ndi Mtima Wosagawanika

Kodi kukhala ndi mtima wosagawanika n’kutani nanga tingatani kuti tipitirize kukhala ndi khalidweli?

Yesetsani Kukhala Ofatsa Kuti Muzisangalatsa Yehova

Kodi Yesu ndi Mose anapereka chitsanzo chotani pa nkhani yokhala ofatsa? Kodi kukhala ofatsa n’kothandiza bwanji masiku ano?

Tizisonyeza Kuti Ndife Oyamikira

Kodi tingaphunzire chiyani kwa Yehova, Yesu ndi Msamaliya wakhate pa nkhani yosonyeza kuyamikira?

Aisiraeli Ankafunika Kusonyeza Chikondi ndi Chilungamo

Kodi Chilamulo cha Mose chimasonyeza chiyani pa mmene Yehova amaonera chikondi komanso chilungamo?

MBIRI YA MOYO WANGA

Makolo Anga Anandithandiza Kuti Ndizitumikira Yehova

Sangalalani ndi mbiri ya moyo wa Woodworth Mills, amene watumikira Yehova mokhulupirika kwa zaka pafupifupi 80.

Kodi Mukudziwa?

Kodi Masunagoge Anayamba Bwanji?