NSANJA YA OLONDA Na. 3 2016 | Kodi Mungatani Munthu Yemwe Munkamukonda Akamwalira?

Munthu aliyense amavutika kwambiri chifukwa cha imfa. Kodi tingatani ngati wachibale kapena mnzathu wamwalira?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Mungatani Munthu Yemwe Munkamukonda Akamwalira

Kodi munthu angatani kuti apirire imfa ya munthu amene ankamukonda? Nanga anthu amene anamwalira angadzakhalenso ndi moyo?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Kumva Chisoni N’kulakwa?

Kodi mungatani ngati ena akuona kuti mukusonyeza chisoni mopitirira malire?

NKHANI YAPACHIKUTO

Zimene Mungachite Ngati Muli Ndi Chisoni

Baibulo limapereka malangizo othandiza kwambiri.

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Tingalimbikitse Bwanji Amene Ali Ndi Chisoni?

Nthawi zina anzake a munthu woferedwa amatha kulephera kudziwa zimene angamuchitire.

NKHANI YAPACHIKUTO

Anthu Amene Anamwalira Adzakhalanso Ndi Moyo

Kodi zimene Baibulo linalonjeza n’zoona?

Kodi Mukudziwa?

Kodi bambo a Yosefe anali ndani? Kodi anthu akale ankagwiritsa ntchito utoto komanso nsalu zotani?

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Ndinayamba Kulemekeza Akazi Komanso Kudzilemekeza

Joseph Ehrenbogen anawerenga mfundo za m’Baibulo ndipo zinamuthandiza kusintha moyo wake.

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

“Inde Ndipita”

Rabeka anali ndi chikhulupiriro komanso makhalidwe ena abwino kwambiri.

Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Kodi kutchula dzina la Mulungu n’kulakwa?

Zina zimene zili pawebusaiti

N’chifukwa Chiyani Anthu Amafa?

Yankho limene Baibulo limapereka pa nkhaniyi ndi lolimbikitsa komanso lopatsa chiyembekezo