NSANJA YA OLONDA Na. 2 2016 | N’chifukwa Chiyani Yesu Anavutika Mpaka Kufa?

Kodi timapindula bwanji chifukwa chakuti cha kuphedwa kwa munthu mmodzi zaka 2,000 zapitazo?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Zinachitikadi?

Kodi timadziwa bwanji kuti zimene Mauthenga Abwino amanena zokhudza Yesu ndi zoona?

NKHANI YAPACHIKUTO

N’chifukwa Chiyani Yesu Anavutika Mpaka Kufa?

Kodi imfa yake ingakuthandizeni bwanji?

Kodi Akhristu Ayenera Kumapemphera mu Akachisi?

Zipembedzo zambiri zikuluzikulu za padzikoli zili ndi akachisi. Kodi kulambira ku akachisi kuli ndi phindu lililonse?

Kumvera Chenjezo Kungapulumutse Moyo Wanu

Maulosi a m’Baibulo amanena momveka bwino zizindikiro zosonyeza kuti Mulungu watsala pang’ono kuwononga dzikoli. Kodi mumvera chenjezo?

Kodi Ndi Ndani Amene Anagawa Machaputala ndi Mavesi a M’Baibulo?

N’chifukwa chiyani anthu ambiri amakonda machaputala ndi mavesi okhala ndi manambala?

Zimene Baibulo Limanena?

Kodi muyenera kuchita mantha ndi Mdyerekezi?

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Yesu Anafera Pamtanda?

Anthu ambiri amaona kuti mtanda ndi chizindikiro cha Chikhristu. Kodi tiyenera kuugwiritsira ntchito polambira?