Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2016

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2016

“Zikomo kwambiri chifukwa magaziniwa ndi a panthawi yake.”—Amy

Amy ndi mayi yemwe amaona kuti nkhani za m’magazini a Galamukani! ndi zothandiza pa moyo wake watsiku ndi tsiku. Mofanana ndi mayiyu, palinso anthu mamiliyoni ambiri amene magaziniwa amawathandiza kwambiri. Pitani pawebusaiti ya www.jw.org/ny kuti muwerenge nkhani zimene zasonyezedwa m’munsimu.

ANTHU AKALE

CHIPEMBEDZO

 • Kodi Baibulo Langokhala Buku Labwino Basi? Na. 2

 • Kodi Baibulo Limalola Kuti Akazi Kapena Amuna Okhaokha Azigonana? Na. 4

 • Kodi Nkhani Yonena za Yesu Ndi Yongopeka? Na. 5

KUCHEZA NDI ANTHU

 • Katswiri Woona za Mmene Ana Osabadwa Amakulira Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake (Y. Hsuuw): Na. 2

KUCHITA ZINTHU NDI ANTHU

 • Kodi Mungasonyezane Bwanji Ulemu? (mwamuna ndi mkazi wake): Na. 6

 • Kodi Mungatani Kuti Mukhale ndi Anzanu Apamtima? Na. 1

 • Kuphunzitsa Mwana Wanu Nkhani Zokhudza Kugonana: Na. 5

 • Mungatani Kuti Musamakangane Pokambirana Mavuto Anu? (mwamuna ndi mkazi wake): Na. 3

 • Zimene Mungachite Mwana Akatsala Pang’ono Kutha Msinkhu: Na. 2

MAYIKO NDI ANTHU

MBONI ZA YEHOVA

 • A Mboni za Yehova Akumasulira M’zinenero Zambiri: Na. 3

 • Kodi Mumadziwa Zotani Zokhudza a Mboni za Yehova? Na. 1

 • “Mfundozi Zindithandiza Kwambiri” (jw.org): Na. 5

NYAMA NDI ZOMERA

 • Mbalame Zokongola Kwambiri: Na. 2

 • Nsomba Yochititsa Chidwi Kwambiri: Na. 6

SAYANSI

 • Chinthu Chodabwitsa (kaboni): Na. 5

 • Kanyama Kam’madzi Komwe Kamasinthasintha Mtundu: Na. 1

 • Khosi la Nyerere: Na. 3

 • Nyenje za Moyo Wautali: Na. 4

 • Ulusi wa Nkhono Yam’madzi: Na. 6

UMOYO NDI MANKHWALA

 • Kodi Kudana ndi Kusagwirizana ndi Zakudya kwa Thupi N’kosiyana Bwanji? Na. 3

 • Kodi Tingapewe Bwanji Matenda? Na. 6

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

ZOSIYANASIYANA

 • Kodi N’zotheka Kusintha Zomwe Munazolowera? Na. 4

 • N’zotheka Kumasangalalabe Ngakhale Muli ndi Mavuto: Na. 1

 • Zimene Mungachite Zinthu Zikasintha: Na. 4