GALAMUKANI! Na. 3 2019 | Baibulo Lingakuthandizeni Kukhala ndi Moyo Wabwino Kwambiri

kwa zaka zambiri, Baibulo lakhala likuthandiza anthu kukhala ndi moyo wabwino kwambiri. Nanunso mukhoza kumakhala wosangalala ngati mutamagwiritsa ntchito malangizo a m’Baibulo pa moyo wanu.

Buku Lakale Lokhala ndi Mfundo Zothandiza Masiku Ano

Taonani zimene ena ananena pa nkhani ya mmene kuphunzira ndi kugwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo kwawathandizira kuti akhale ndi moyo wabwino.

Moyo Wathanzi

Mfundo za M’Baibulo zingatithandize kuti tizisamalira thanzi lathu.

Mtendere wa M’maganizo

Timakhala ndi mtendere wa m’maganizo tikamayesetsa kukhala odziletsa.

Banja Labwino Komanso Mabwenzi Abwino

Tikhoza kukhala ndi anzathu abwino tikamaganizira kwambiri zimene tingawachitire m’malo mwa zimene iwowo angatichitire.

Kugwiritsa Ntchito Bwino Ndalama

Kodi mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni bwanji kupewa mavuto a zachuma?

Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu

Werengani nkhaniyi kuti muone mmene malamulo a Mulungu komanso mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kuti mukhale pa ubwenzi ndi Mulungu.

Palibenso Buku Lothandiza Kwambiri Kuposa Baibulo

Kafukufuku amasonyeza kuti Baibulo ndi buku lomwe limafalitsidwa komanso kumasuliridwa m’zinenero zambiri kuposa buku lina lililonse.

Zimene Zili M’magaziniyi: Baibulo Lingakuthandizeni Kukhala ndi Moyo Wabwino Kwambiri

Baibulo lili ndi mfundo zabwino zomwe zingatithandize kukhala ndi moyo wabwino.