GALAMUKANI! Na. 3 2016 | A Mboni za Yehova Akumasulira M’zinenero Zambiri

A Mboni za Yehova akugwira ntchito yofunika kwambiri yomasulira mabuku.

NKHANI YAPACHIKUTO

Ntchito Yomasulira Yathetsa Vuto la Kusiyana Zinenero

Kodi n’chifukwa chiyani a Mboni za Yehova akumasulira m’zinenero zambiri?

NKHANI YAPACHIKUTO

A Mboni za Yehova Akumasulira M’zinenero Zambiri—Zimene Zimachitika Pomasulira

Womasulira akufotokoza mmene amagwirira ntchito.

TIONE ZAKALE

Ignaz Semmelweis

Mabanja onse akuyenera kumuthokoza kwambiri munthu ameneyu. Chifukwa chiyani?

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Mungatani Kuti Musamakangane Pokambirana Mavuto Anu?

Amuna ndi akazi amafotokoza maganizo awo mosiyana. Kudziwa mfundoyi kungakuthandizeni kuti musamakangane.

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Chikhulupiriro

Baibulo limanena kuti ‘popanda chikhulupiriro n’zosatheka kukondweretsa Mulungu.’ Chikhulupiliro n’chiyani? Mungatani kuti mukhale ndi chikhulupiriro?

Kodi Kudana ndi Kusagwirizana ndi Zakudya kwa Thupi N’kosiyana Bwanji?

Kodi kungoganiza kuti muli ndi vuto n’kuthamangira kusiya zakudya zinazake kuli ndi mavuto otani?

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Khosi la Nyerere

Kodi zimatheka bwanji kuti nyerere izinyamula zinthu zolemera kwambiri?

Zina zimene zili pawebusaiti

‘Uthenga Wabwino Ukulalikidwa Kudziko Lililonse, Fuko Lililonse ndi Chinenero Chilichonse’

Pamafunika kumasulira molondola choonadi cha m’Baibulo kuti anthu ambiri achidziwe. Kodi ntchito imeneyi imagwiridwa bwanji? Kodi anthu omasulira amakumana ndi mavuto otani?