Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

GALAMUKANI! Na. 2 2021 | Kodi Zipangizo Zamakono Zimakulamulirani?

Kodi zipangizo zamakono zimakulamulirani? Ambiri akhoza kunena kuti amazigwiritsa ntchito moyenera ndipo siziwalamulira. Koma pang’ono ndi pang’ono, zipangizo zamakono zikhoza kusokoneza anthu m’njira yoti sangathe kuizindikira.

Kodi Zipangizo Zamakono Zimakhudza Bwanji Ubwenzi Wanu ndi Anthu Ena?

Zipangizo zamakono zingakuthandizeni kuti mukhale ndi anzanu abwino komanso kuti mukhale nawo pa ubwenzi wolimba.

Kodi Zipangizo Zamakono Zimakhudza Bwanji Ana Anu?

Ana savutika kugwiritsa ntchito zipangizo zamakono koma amafunika kuthandizidwa.

Kodi Zipangizo Zamakono Zimakhudza Bwanji Banja Lanu?

Mwamuna ndi mkazi wake akamagwiritsa ntchito moyenera zipangizo zamakono akhoza kulimbitsa ubwenzi wawo.

Kodi Zipangizo Zamakono Zimakhudza Bwanji Mmene Mumaganizira?

Zikhoza kukhudza luso lanu la kuwerenga, zingachititse kuti muzivutika kuika maganizo pa chinthu chimodzi komanso zingakhudze zimene mumachita mukakhala kwanokha. Mfundo zitatu zimene zingakuthandizeni kuti muziganiza bwino.

Dziwani Zambiri pa JW.ORG

Kodi ndi nkhani iti imene mukufuna kuidziwa bwino?

Zimene Zili M’magaziniyi

Ganizirani njira zina zovuta kuzizindikira zimene zingakhudze maubwenzi anu ndi anzanu, banja lanu komanso kaganizidwe kanu mukamagwiritsa ntchito zipangizo zamakono.