Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Xuanyu Han/Moment via Getty Images

Zimene Zili M’magaziniyi

Zimene Zili M’magaziniyi

Dzikoli lili pangozi.

Kodi likhalanso bwino kapena lizingoipiraipirabe mpaka kuwonongekeratu limodzi ndi zamoyo zonse? Werengani nkhani zimene zili m’magaziniyi kuti mudziwe zimene zikuchitikira dzikoli komanso ngati pali zifukwa zilizonse zotichititsa kukhala ndi chiyembekezo.

Kodi tsogolo la dzikoli ndi lotani pa nkhani ya:

  • Madzi abwino?

  • Nyanja zikuluzikulu?

  • Nkhalango?

  • Mpweya?