Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi mukufuna kudziwa zambiri?

Kodi mukufuna kudziwa zambiri?

Munthu wina wanzeru analemba kuti: “Nzeru ndiyo chinthu chofunika kwambiri. Peza nzeru, ndipo pa zinthu zonse zimene upeze, upezenso luso lomvetsa zinthu.” (Miyambo 4:7) Mlengi wathu amatithandiza kuti tikhale ndi nzeru komanso kuti tizimvetsa bwino zinthu n’cholinga choti tizisankha zinthu mwanzeru n’kumakhala ndi moyo wosangalala.

Ngati mukufuna kudziwa zambiri zokhudza nzeru zothandiza zomwe zimapezeka m’Baibulo, pitani pa jw.org. Pamenepa mupezapo zinthu monga . . .

  • BAIBULO

  • MAVIDIYO

  • MAKATUNI

  • ZOCHITIKA PA MOYO WA ANTHU ENA

  • NKHANI

Zonsezi zikupezeka mwaulere ndipo ndi zothandiza kwa anthu a misinkhu yonse komanso ochokera kulikonse.