GALAMUKANI! Na. 1 2016 | N’zotheka Kumasangalalabe Ngakhale Muli Ndi Mavuto

Kodi mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kuti muzisangalala?

NKHANI YAPACHIKUTO

N’zotheka Kumasangalalabe Ngakhale Muli Ndi Mavuto!

Kodi mfundo za m’Baibulo zingakuthandizeni kuti muzisangalala?

Kodi Mumadziwa Zotani Zokhudza a Mboni za Yehova?

Onani mfundo izi kuti mupeze mayankho a mafunso.

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Kodi Mungatani Kuti Mukhale ndi Anzanu Apamtima?

Mfundo 4 zomwe zingakuthandizeni kuti mupeze anzanu apamtima.

ANTHU NDI MAYIKO

Dziko la Liechtenstein

N’chiyani chimakopa anthu ambiri okaona malo m’dziko laling’ono ngati limeneli?

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Kumwamba

Kodi anthu onse abwino amapita kumwamba akamwalira?

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Kanyama Kam’madzi Komwe Kamasinthasintha Mtundu

Akatswiri akutengera kanyamaka kuti apange zovala zotha kusinthasintha mitundu mofulumira kwambiri.

Zina zimene zili pawebusaiti

Kodi Chimachitika N’chiyani Munthu Akamwalira?

Kodi munthu akamwalira amadziwa zinthu zimene zikuchitika?