Chichewa
Musadzaphonye Kuwerenga Galamukani! Yotsatira
/assets/ct/7e6416ec85/images/syn_placeholder_sqr.png

Musadzaphonye Kuwerenga Galamukani! Yotsatira

Musadzaphonye Kuwerenga Galamukani! Yotsatira

Kuyambira ndi Galamukani! ya January 2013, magazini ya Galamukani! izikhala ndi nkhani zosavuta kuwerenga, zithunzi zokongola komanso nkhani zina ngati: “Mfundo Zothandiza Mabanja,” “Kucheza ndi Anthu,” “Anthu Komanso Komwe Akuchokera” ndi “Zithunzi Zakale.” *

Nkhani zimene zidzatuluke mu Galamukani! ya January 2013

Mfundo Zothandiza Mabanja​—“Zimene Mungachite Kuti Muzilankhulana Momasuka ndi Mwana Wanu Wachinyamata”

Kucheza ndi Anthu​—“Wasayansi Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake”

Anthu Komanso Komwe Akuchokera​—“Dziko la Cameroon”

^ ndime 2 Nkhani zina sizizidzatuluka mwezi uliwonse.