Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2012

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2012

CHIPEMBEDZO

 • Baibulo Ndi Buku la Maulosi Olondola, 5/12, 6/12, 7/12, 8/12, 9/12, 10/12, 11/12, 12/12

 • Zimene Zingakuthandizeni Kulimvetsa Baibulo, 11/12

MAUNANSI A ANTHU

 • Kodi Mwana Wanu Amaopa Zoopsa Zomwe Zachitika? 10/12

 • Kufuna Kudzipha, 1/12

 • Kukhala Kholo Labwino, 10/12

 • Kuleza Mtima, 12/12

 • Kupsa Mtima, 3/12

 • Kuthandiza Mwana Yemwe Wachibale Wake Wamwalira, 7/12

 • Kuthandiza Odwala Matenda Oda Nkhawa, 3/12

 • Mabanja Omwe Ali Ndi Ana Opeza, 4/12

 • Makolo Omwe Akulera Okha Ana, 11/12

 • Malo Ochezera a pa Intaneti, 2/12

 • Muzikumbukira Kunena Kuti Zikomo Kwambiri, 7/12

MAYIKO NDI ANTHU

 • Batik—Nsalu Zokongola za ku Indonesia, 6/12

 • Caucasus Dera Lamapiri Komanso Zilankhulo Zosiyanasiyana, 12/12

 • Chiarabu Chinali Chinenero cha Anthu Ophunzira Kwambiri, 2/12

 • Chipatso Chokoma Kwambiri cha ku Armenia, 3/12

 • Chitoliro (Switzerland), 1/12

 • Kuteteza Zachilengedwe Kuti Zisatheretu (New Zealand), 4/12

 • Mpira wa EURO 2012 (Poland, Ukraine), 6/12

 • Mzinda wa Mapepala (Czech Republic), 2/12

 • Nkhondo ya ku Ain Jalut (Mongolia), 3/12

 • Nkhumba N’zofunika kwambiri (Papua New Guinea), 8/12

 • Nyumba Zachitetezo za ku Terezín (Czech Republic), 3/12

MBIRI YA MOYO WA ANTHU

 • Kukhala Bwenzi la Mulungu Ngakhale Utakalamba (O. Mattila), 1/12

 • Ndinkakonda Kuchita Zachiwawa (S. Garza), 8/12

 • Sanataye Nane Mtima (K. Lyons), 11/12

 • Tsopano Ndili Ndi Mtendere Wamumtima (E. Nahakbria), 6/12

MBONI ZA YEHOVA

 • Buku lachingelezi la Young People Ask, Volume I, 6/12

 • Galamukani! Yotsatira, 12/12

 • Msonkhano Wachigawo Wakuti, “Tetezani Mtima Wanu,” 5/12

 • Njira Zochizira Popanda Kuika Magazi (Russia), 9/12

 • Nyumba za Ufumu Zomwe Zamangidwa ku Malawi, 5/12

NYAMA NDI ZOMERA

 • Anyani a Chiyendayekha, 10/12

 • Bakha Wam’madzi, 11/12

 • Chipatso Chokoma Kwambiri cha ku Armenia, 3/12

 • Duwa Lalikulu Padziko Lonse, 8/12

 • Kodi Mumadya Bowa? 3/12

 • Kodi Munaonapo Ng’ombe Ngati Iyi? 12/12

 • Kodi N’zotheka Kuteteza Zachilengedwe Kuti Zisatheretu? 4/12

 • Koma Ndiye Chimphunotu! 5/12

 • Malo Osungira Nyama, 9/12

 • Mandimu, 9/12

 • Ndiwo Zokoma, 6/12

 • Nkhalango ya Tasmania, 4/12

 • Nkhanu Zam’nyanja, 7/12

 • Nkhumba, 8/12

 • Nsikidzi, 12/12

UMOYO NDI MANKHWALA

 • Akatswiri Akale a Zamankhwala, 9/12

 • Kunenepa Kwambiri, 10/12

 • Kusamalira Zakudya, 6/12

 • Matenda Oda Nkhawa, 3/12

 • Mtedza wa Betel, 2/12

 • Nyamakazi ya M’mafupa, 8/12

SAYANSI

 • Akatswiri Akale a Sayansi ya Zakuthambo, 4/12

 • Akatswiri Akale a Zamankhwala, 9/12

 • Akatswiri Akale Opanga Makina, 11/12

 • Chiarabu Chinali Chinenero Cha Anthu Ophunzira Kwambiri, 2/12

 • Kodi Zinangochitika Zokha? 1/12, 2/12, 3/12, 4/12, 5/12, 6/12, 7/12, 8/12, 9/12, 10/12, 11/12

 • Nyenyezi, 2/12

ZACHUMA NDI NTCHITO

 • Kodi Kuchita Zinthu Mwachilungamo N’kothandiza? 1/12

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

 • “Choonadi Chidzakumasulani,” 5/12

 • Kodi Akufa Angathandize Amoyo? 6/12

 • Kodi Mulungu Amagwiritsa Ntchito Masoka Achilengedwe Kulanga Anthu? 12/12

 • Kodi Mumakhulupirira Nyenyezi? 10/12

 • Kodi Mumaona Kuti Chipembedzo N’chofunika? 9/12

 • Kodi Muyenera Kupita Pamalo Enaake Kuti Mukapemphere? 8/12

 • Kodi Ndani Angasinthe Zinthu Padzikoli? 7/12

 • Kodi Tizivomereza Khalidwe Logonana Amuna Kapena Akazi Okhaokha? 1/12

 • Kudzionetsera, 11/12

 • Kukhala pa Mtendere ndi Ena, 3/12

 • N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuyamikira Ena? 4/12

 • Tizitchula Zinthu Ziti Tikamapemphera Kwa Mulungu? 2/12

ZOTI BANJA LIKAMBIRANE

 • 1/12, 2/12, 3/12, 4/12, 5/12, 6/12, 7/12, 8/12, 9/12, 10/12, 11/12, 12/12

ZOCHITIKA PA DZIKO

 • Chenjerani Ndi Zigawenga za pa Intaneti, 5/12

 • Kodi Zinthu Zidzasinthadi Padzikoli? 7/12

 • Ndani Angamve Kulira kwa Oponderezedwa? 5/12

 • Umbava wa pa Intaneti, 1/12

 • Zachiwawa, 8/12

ZOSIYANASIYANA

 • Dikishonale Yomwe Yatha Zaka 90 Ikulembedwa, 12/12

 • Gwiritsani Ntchito Maso Anu Mwanzeru, 2/12

 • Kubera Mayeso, 8/12

 • Kutha kwa Dziko, 9/12

 • Sitima ya Titanic, 4/12

 • Zimene Mungachite Kuti Zizikuyenderani ku Sukulu, 10/12

ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA

 • Kaya Ndinaneneranji Zimene Zija? 1/12

 • Kodi Mwamuna Weniweni Amakhala Wotani? 12/12

 • Kodi Ndimangocheza Naye Kapena Ndimamufuna? 6/12, 7/12

 • Kodi Ndimatengera Chitsanzo cha Ndani? 8/12

 • Kodi Ndingatani Kuti Ndizisangalala Ndikamawerenga Baibulo? 2/12

 • Kodi Ndingatani Ngati Ndapanikizika Maganizo? 11/12

 • Kodi Ndiziyembekezera Chiyani M’banja? 9/12, 10/12

 • Kodi Pali Vuto Lililonse Kukhala Wotchuka? 3/12

 • N’chifukwa Chiyani Makolo Anga Samandimvetsa? 5/12

 • N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kumapita ku Misonkhano ya Mpingo? 4/12