Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2011

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2011

 Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2011

NYAMA NDI ZOMERA

Nyama Zokongola Mogometsa (Mahatchi a ku Arabia), 4/11

Mbalame N’zaluso pa Usodzi, 9/11

Khungwa la Mtengo, 7/11

Uchi wa Nyerere, 5/11

ZACHUMA NDI NTCHITO

Muzigwiritsa Ntchito Ndalama Mwanzeru, 9/11

ZOTI BANJA LIKAMBIRANE

1/11, 2/11, 3/11, 4/11, 5/11, 6/11, 7/11, 8/11, 9/11, 10/11, 11/11, 12/11

UMOYO NDI MANKHWALA

Khansa ya M’mawere, 8/11

Ngati Mwana Ali ndi Khansa, 5/11

Ana Obadwa ndi Matenda Ozerezeka, 6/11

Matenda a Chingwangwa, 11/11

Mfundo Zisanu Zokuthandizani Kukhala ndi Thanzi Labwino, 3/11

Kusamalira Mwapadera Munthu Wodwala Matenda Oti Sachira, 7/11

Mutu Waching’alang’ala, 1/11

Matenda a Pulositeti, 2/11

Kugona Mokwanira, 1/11

Nzeru Zothandiza Munthu Kukhala ndi Thanzi Labwino, 8/11

MAUNANSI A ANTHU

Kodi Mungaiwale Bwanji Imfa ya Munthu amene Mumamukonda? 4/11

Kulera Ana Kuti Akule Bwino, 10/11

Kulera Ana Obadwa ndi Matenda Ozerezeka, 6/11

MBONI ZA YEHOVA

Buku la Phunzirani kwa Mphunzitsi Waluso, 12/11

“Sindinkafuna Kulisiya” (Buku la Zimene Achinyamata Amadzifunsa, Gawo 2), 4/11

“Ufumu wa Mulungu Ubwere” Msonkhano Wachigawo, 5/11

“Mulembereni Kalata Anton” (Russia), 9/11

MAYIKO NDI ANTHU

Madzi osefukira ku Japan 2011, 12/11

Buku Lachiweruzo (England), 9/11

Uchi wa Nyerere (Australia), 5/11

Maulendo a Ibn Battuta, 8/11

Munthu Wokonda Kufunsa Mafunso (Nicarao wa ku Nicaragua), 12/11

Anatchona Kofunafuna Golide (Australia), 2/11

John Foxe Anakhala ndi Moyo pa Nthawi Yovuta Kwambiri (England), 11/11

Nsanja Zokongola za M’mapiri a Svaneti (Georgia), 6/11

Chakumwa cha ku Mexico (tequila), 11/11

Nyumba za Mbalame za ku Istanbul (Turkey), 1/11

Mathithi a Murchison Ndi Okongola Kwambiri (Uganda), 9/11

Luso la Zopangapanga la Anthu a ku Russia, 9/11

Zida Zoimbira za M’nthawi ya Aisiraeli, 3/11

Anthu a Mtundu wa Chitata, 9/11

Zojambula Zosangalatsa za Tingatinga (Tanzania), 11/11

Njira Yomwe Akapolo Ankadutsa (Benin), 5/11

Abusa a Nkhosa a ku Wales, 7/11

MBIRI YA MOYO WA ANTHU

Ndinadziwa Yemwe Adzathetse Kupanda Chilungamo (U. Menne), 11/11

Ndinali Munthu Woopsa Kwambiri (J. Nebrera), 4/11

Ndimasangalala Kuti Ndine M’busa (A. Bekmanov), 3/11

Moyo Wopindulitsa Kwambiri (H. Neuhardt), 2/11

Chipani cha Nazi Chinalephera Kundisintha (H. Liska), 8/11

Ndinapeza Chinthu Chamtengo Wapatali (M. Ibatullin), 6/11

ZOSIYANASIYANA

Ngozi Zapamsewu, 7/11

Mwana Akamabadwa, 1/11

Zolinga Zimene Mungathe Kuzikwaniritsa, 2/11

Mawotchi Amakedzana (mawotchi), 1/11

Mulungu Adzathetsa Mavuto Athu Onse, 7/11

Milomo Yanu Ndi “Ziwiya Zamtengo Wapatali,” 5/11

Nyimbo, 8/11

Zamatsenga, 2/11

Nyengo Inalepheretsa Anthu Kupambana Nkhondo Zikuluzikulu, 6/11

CHIPEMBEDZO

Zifukwa Zomveka Zokhulupirira Kuti Kuli Mulungu 11/11

Buku Limene Lapulumuka Zambiri (Baibulo), 12/11

Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira (Baibulo), 1/11, 2/11, 3/11, 4/11, 5/11

Mtengo wa Khirisimasi, 12/11

Kodi Zipembedzo Zikuthandiza Kuti Anthu Azikhala Mwamtendere? 1/11

“Musaganize Kuti Ndamwalira,” 9/11

Buku la Jean Crespin Lonena za Anthu Ofera Chikhulupiriro, 3/11

Baibulo la King James, 12/11

SAYANSI

Moyo ndi Mphatso Yamtengo Wapatali, 5/11

Kodi Zinangochitika Zokha? 1/11, 2/11, 3/11, 4/11, 5/11, 6/11, 8/11, 9/11, 11/11

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Kodi Baibulo Limalimbikitsa Ukapolo? 7/11

Kodi Chikhulupiriro ndi Kuganiza Mwakuya Zimayenderana? 1/11

Kodi Mulungu Amasamalira Nyama? 12/11

Kodi Mulungu Ali Paliponse? 4/11

N’chifukwa Chiyani Mulungu Salola Akhristu Kumenya Nkhondo? 8/11

Zimene Mungachite Kuti Banja Lanu Liziyenda Bwino, 11/11

Kodi Sayansi ndi Baibulo Zimagwirizana? 2/11

Kudzizunza, 3/11

Kodi Tiziona Kuti Tsiku Lina Pamlungu Ndi Lopatulika? 9/11

Kodi Mumafuna Kuti Mwana Wanu Adzakhale Wotani Akadzakula? 10/11

N’chifukwa Chiyani Akhristu Oona Amadedwa? 5/11

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusamala ndi Zimene Timalankhula? 6/11

ZOCHITIKA PA DZIKO

Zokambirana Zokhudza Kusokonekera kwa Nyengo, 11/11

Zauchigawenga, 6/11

ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA

Kodi Ndimagwiritsira Ntchito Foni, Tv, Kompyuta Kapena Intaneti Mopitirira Malire? 1/11

Kodi Ndine Wolephera? 5/11

Kodi Ndingatani Kuti Anthu Azindikonda Ndikangokumana Nawo Koyamba? 6/11

Malo Ochezera a pa Intaneti, 7/11, 8/11

Kodi Chimafunika N’chiyani Kuti Phwando Likhale Losangalatsa? 12/11

Kodi Ndiyenera Kudziwa Chiyani Zokhudza Kusuta Fodya? 3/11

Kodi Ndi Anthu Ati Amene Ndingamacheze Nawo Momasuka? 4/11

Kodi Ndingasankhe Bwanji Mafilimu, Mabuku Komanso Nyimbo Zabwino? 11/11

Kodi Ndimadziwa Mfundo Zimene Ndimayendera? 10/11

Kodi Ndingadziwe Bwanji Anzanga Enieni? 9/11

N’chifukwa Chiyani Makolo Anga Sandilola Kupita Kokasangalala? 2/11