Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mlozera Nkhani wa Magazini A Galamukani! a 2006

Mlozera Nkhani wa Magazini A Galamukani! a 2006

 Mlozera Nkhani wa Magazini A Galamukani! a 2006

BAIBULO

Baibulo la M’chinenero Chamakono

CHIPEMBEDZO

Halowini, 10/06

Kodi Angelezi Oyambirira Kusamukira ku America Anali Akristu Oona? 2/06

Kodi Yesu Anali Ndani? 12/06

Kuyankha Funso Lovuta Kwambiri Loti “Chifukwa Chiyani?” 11/06

Michael Agricola (womasulira Baibulo), 1/06

Michael Servetus Anafufuza Choonadi Yekhayekha, 5/06

Mulungu Anagwiritsa Ntchito Chisinthiko? 9/06

MAUNANSI A ANTHU

Ana Ofunika Kuwasamalira Mwapadera, 4/06

Chikondi, 3/06

Kuthandiza Mwana Wanu Wamkazi Kukonzekera Kutha Msinkhu, 5/06

Mmene Mungakhalire ndi Banja Losangalala, 7/06

“Nthawi ya Chakudya Imatithandiza Kukondana,” 11/06

MAYIKO NDI ANTHU

Alhambra (ku Spain), 2/06

Aromani (Majipise), 10/06

Calypso—Nyimbo Zamakolo za ku Trinidad, 12/06

Chernobyl (ku Ukraine), 4/06

Chigwa Chotchedwa Death Valley (ku California), 11/06

Chilumba Chokongola Kwambiri cha Mchenga (Chilumba cha Fraser), 3/06

Mekong (mtsinje, wa ku Asia), 11/06

Michael Agricola “Anasintha Zinthu Kwambiri” (ku Finland), 1/06

Mlatho wa Tower Bridge Ndi Njira Yolowera mu London, 10/06

Mtsinje wa Thames (ku England), 2/06

Munda Wokongola Mogometsa (Gaudeloupe, ku Martinique), 5/06

Ulendo Wokaona Nkhosa Zam’tchire (ku Cyprus), 3/06

“Unabadwa kwa Makolo Oyera Kuposa Onse” (kupanga mchere, ku Brazil), 12/06

Uthenga Uyenera Kuperekedwa (kwa a Inca), 7/06

MBIRI YA MOYO WA ANTHU

Anakonda Zimene Anaphunzira, 12/06

Chikhulupiriro Chandithandiza Kupirira Matenda Oopsa (J. Stuart), 1/06

‘Ndidzadumpha Ngati Nswala’ (F. Abbatemarco), 8/06

‘Ndikufuna Kutumikira Mulungu Ndisanafe’ (M. Free), 3/06

Ndinali Mwana Wolowerera (M. W. Sunday), 12/06

Ndinali Wotaya Mtima Koma Tsopano Ndine Wosangalala (V. González), 7/06

Ndinaphunzira Kudalira Mulungu (E. Toom), 4/06

Ndinapulumutsidwa ku Masautso (J. François), 11/06

MBONI ZA YEHOVA

“Anaikidwa M’ndende Chifukwa cha Chikhulupiriro Chawo” (ku Auschwitz), 4/06

Chikhulupiriro cha Mwana (wodwala khansa), 8/06

Kumvera Machenjezo (Mphepo Yamkuntho ya Katrina), 6/06

Kuthandiza Mtsikana Wovutika Maganizo, 10/06

Kwa Owerenga (Galamukani!), 1/06

Misonkhano Yachigawo Yakuti “Chipulumutso Chayandikira,” 6/06

Mphatso ya Mtengo Wapatali (Buku la Mphunzitsi Waluso), 12/06

“Mumakondwerera Tsiku la Agogo Aakazi?” 12/06

“N’kabwino Kwabasi!” (kabuku ka ‘Onani Dziko Lokoma’), 2/06

“N’labwino Kwambiri” (Buku la Baibulo Limaphunzitsa Chiyani), 11/06

SAYANSI

Chifukwa Chimene Timakhulupirira Kuti Kuli Mlengi, 9/06

‘Katswiri wa ku Britain Yemwe Anaiwalika’ (Robert Hooke), 7/06

Kodi Chisinthiko Chinachitikadi? 9/06

Kodi Mlengi Alipo? 9/06

Kukambirana ndi Katswiri wa Sayansi, 9/06

Maselo Ofiira a M’magazi, 1/06

Mukhoza Kukhala ndi Moyo Wautali Bwanji? 5/06

N’chifukwa Chiyani Madzi a M’nyanja Zikuluzikulu Amakhala Amchere? 7/06

UMOYO NDI MANKHWALA

Kodi Kusisita Mwana N’kofunika? 7/06

Kulandira Mafoni Angozi—ku London, 3/06

Kupirira Matenda Oopsa, 1/06

Malo Opangira Ziwalo, 2/06

N’chifukwa Chiyani Magazi Ali Ofunika Kwambiri? 8/06

Nkhungu Imathandiza Komanso Imawononga 1/06

Nsomba Zikakudwalitsani, 7/06

Ukalamba, 2/06

ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA

Kucheza ndi Anzanga a ku Sukulu, 4/06

Muli Ndi Matenda Ovutika Kudya? 10/06

N’chifukwa Chiyani Amandiikira Malamulo Ambirimbiri? 12/06

N’chifukwa Chiyani Ndimadzivulaza? 1/06

Ndidzagwire Ntchito Yotani Pamoyo Wanga? 7/06

Ndingafotokoze Bwanji Zimene Ndimakhulupirira Zokhudza Chilengedwe? 9/06

Ndingapewe Bwanji Zogonana Kusukulu? 3/06

Ndingatani Kuti Ndisiye Kudzivulaza? 2/06

Ndingatani Kuti Ndizisamala Ndalama? 6/06

Ndingathandize Bwanji Anthu Amene Akufunika Thandizo? 8/06

Ndingathetse Bwanji Chizolowezi Chimenechi? (kudziseweretsa maliseche), 11/06

Ndiziwerenga Chifukwa Chiyani? 5/06

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Anthu Akafa Amasanduka Angelo? 8/06

Kodi Mungathe Kuthandiza Anthu Akufa? 10/06

Kukhala Munthu Wamtendere N’kothandiza? 5/06

Kumwa Mowa, 12/06

Mzimu Woyera Ndi Munthu? 7/06

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kudalira Baibulo Kuti Lizititsogolera? 1/06

Ngati Anthu Akukondana Ndiye Kuti Palibe Cholakwika Atagonana Asanakwatirane? 11/06

Pali Mulungu Mmodzi Yekha Woona? 2/06

Sayansi Imatsutsana ndi Nkhani ya mu Genesis? 9/06

Tchimo Loyambirira Linali Chiyani? 6/06

Yesu Anaferadi Pamtanda? 4/06

Yesu Analidi Mwana wa Mulungu? 3/06

ZINYAMA NDI ZOMERA

Abulu, 12/06

Basi Adutsa! (atsekwe), 1/06

Dongosolo Lodabwitsa la Zomera, 9/06

Masiponji, 5/06

Mbalame za M’mphepete mwa Nyanja, 8/06

Nkhosa Zam’tchire, 3/06

Nthanga Imene Inazungulira Dziko (khofi), 3/06

ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE

Uchigawenga, 6/06

ZOSIYANASIYANA

Bwato la ku Galileya, 8/06

Chimwemwe, 4/06

Kodi M’tsogolo Muli Zotani? 1/06

Kuba Magalimoto, 10/06

Kujambula Zithunzi, 6/06

Silika, 6/06

TV, 10/06

Zimene Mumakhulupirira Zili ndi Ntchito? 9/06